Social Growth

Social Growth DAILY NEWS UPDATES

🇲🇼follow us for Dairy
trending news updates📷
🎙️Inbox for music & business promo 🎼

05/09/2025

Tamia ja Vs Vj ken official

mwati zatani 😂

04/09/2025

mwadzuka bwanji abale?

akutsatsa njinga munthuyi 😁Sept. Sipatali azanga lekani kuyenda wapansi kunja kwa dzuwa uku katundu apite moyo usale. Az...
03/09/2025

akutsatsa njinga munthuyi 😁
Sept. Sipatali azanga lekani kuyenda wapansi kunja kwa dzuwa uku katundu apite moyo usale. Azanga tengani katundu uyu k230,000 inbox me ndili Lilongwe. Discount ilipo. This is good for madam.

02/09/2025

musadagone tapangani share page yanthu kwazizanu tidzadzane pano 🥰

wadzipha dzulo lija ndi uyu anangolemba post pa status yake kt no peace no life 👐
02/09/2025

wadzipha dzulo lija ndi uyu anangolemba post pa status yake kt no peace no life 👐

02/09/2025

lNU MULIPATI👇👇
DPP
MCP
UDF
UTM

02/09/2025

Kiss 👄nde kusimzinira ku Church
Akat tipemphere
Zimaso tong'otong'o🥺💔🤌

akt kosakila money 💰🤑 sasakha km kodyela 😂😂 girls ulemuwanu 🙊
01/09/2025

akt kosakila money 💰🤑 sasakha km kodyela 😂😂 girls ulemuwanu 🙊

ngati pali makolo awo pano alangizen anawa 🥺
01/09/2025

ngati pali makolo awo pano alangizen anawa 🥺

01/09/2025


Mwana wasukulu waku CU wazimangilila😢💔

 Bungwe la Malawi Snake Rescue lapempha anthu kuti asiye kupha njoka chifukwa ndi mbali imodzi ya chilengedwe cha dziko ...
01/09/2025



Bungwe la Malawi Snake Rescue lapempha anthu kuti asiye kupha njoka chifukwa ndi mbali imodzi ya chilengedwe cha dziko lino.

Mmodzi wa akuluakulu a bungweli, a Anaclete Josen, wapereka pempholi njoka ina ya mtundu wa mamba itafa pamene amaseyera kupulumutsa moyo wake.

A Josen ati njokayi anakayigwira pa malo ena ku Natural Resources College m’boma la Lilongwe ndipo pa nthawiyi anthu anali atayitema ndi zikwanje komanso agalu anali atayiluma.

Iwo ati akatswiri osamalira njoka anayesera kusoka mabala a njokayi koma ululu wa kulumidwa ndi agalu ndi umene unachititsa kuti ife.

A Josen, amene amaphunzitsa ku Catholic University m’boma la Chiradzulu, ati anthu akawona njoka asamaziphe ndipo mmalo mwake aziyitana akatswiri kuti akazigwire.

“Munthu amene akuyesera kupha njoka amakhalanso pa chiwopsezo chakuti akhoza kulumidwa pamene njokayo ikuyesera kudziteteza.

Choncho kuyesera kupha njoka ndi kuyika moyo pa chiswe,” iwo anatero.

A Josen anati njoka zimathandiza kuchepetsa chiwerengero cha makoswe komanso amazigwiritsa ntchito popanga mankhwala.

follow Growth

Address

Pretoria

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Social Growth posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share