Shaqar the artist

Shaqar the artist Content creator,storyteller & artist ๐Ÿ‡ฟ๐Ÿ‡ฆ ๐Ÿ‡ฒ๐Ÿ‡ผ ๐Ÿ‡ณ๐Ÿ‡ฌ

Rule number 1Bro code: Do not mock a brother to entertain the table, thank you!Good morning
19/09/2026

Rule number 1

Bro code: Do not mock a brother to entertain the table, thank you!

Good morning

Mulibwanji?
16/09/2026

Mulibwanji?

Hello everyone I'm fully back๐Ÿ’ฏThank you Facebook teamโœ…๏ธ
13/09/2026

Hello everyone I'm fully back๐Ÿ’ฏ

Thank you Facebook teamโœ…๏ธ

Eeeeh nde mukuti Jane Make Thembie page yake yafika over 30k followers nthawi yomwe ndinasowayi? Mwati sanagwidwe ndi ma...
12/09/2026

Eeeeh nde mukuti Jane Make Thembie page yake yafika over 30k followers nthawi yomwe ndinasowayi? Mwati sanagwidwe ndi markzukerberg uyu.

Zambiri zachitika, mafriends ena tinaluza ndipo ena anayesetsabe kukhala nafe mpaka lero.

Thanks to everyone ๐Ÿ’ฏ koma Jane zikuonetsa ngati anapeza wina๐Ÿ˜” ayi zikomo

Stop spreading fake stories.1:Bolo young analibe group iliyonse yazamaliro Yes koma patayambika kusonkha within 24hrs pa...
08/07/2026

Stop spreading fake stories.

1:Bolo young analibe group iliyonse yazamaliro
Yes koma patayambika kusonkha within 24hrs panapezeka 5million ndipo pasapezeke onena kuti amamgoonjoya analibe ndalama no ndalama zasonkhedwa mwachanguso anali ndi fan base yambiri.

2 bolo young anali ndi akazi ambiri.
No kungoti amatha kucheza kwambiri ndipo analibe hate ndi anthu ambiri azimayi amamufira cos looks yabho dressing mbambande plus gym basitu.

Komaso ex wamzeru ngati Vanessa pink wasokha 1 million no matukutuku.

Ngati unalibe kuthekera kothandizira pazovutazi ndibwino kumangoona cos chobwera mawa sizimadziwika tsiku lochoka padziko pano amadziwa ndi mulungu ndipo njira ya imfa yomwe izatitengere amaziwa ndi mwini namalenga.

Palibe azafike zaka 200 tonse tizalawa imfa.

Rest in peace madhla๐Ÿ’”๐Ÿ•Š

Tsono mzangayu kujoniko nde amasangalalako tikumakuonanitu mu ma social media koma kumudzi muli nyumba inu? Kapena muzik...
07/07/2026

Tsono mzangayu kujoniko nde amasangalalako tikumakuonanitu mu ma social media koma kumudzi muli nyumba inu? Kapena muzikalakhula chi Xhosa pansi pamtengo๐Ÿ˜„๐Ÿ˜„

Eeeeh ayi zikomo ๐Ÿšถโ€โ™‚๏ธ๐Ÿšถโ€โ™‚๏ธndiangati mwamupanga follow lero mzangayu Jane Make Thembie ๐Ÿ™Œ

Sheโ€™s heartbroken ๐Ÿ’” at the moment, poluza bolo young yemwe anali boyfriend wake.Was secret dating and it was massive ndi...
03/07/2026

Sheโ€™s heartbroken ๐Ÿ’” at the moment, poluza bolo young yemwe anali boyfriend wake.

Was secret dating and it was massive ndipo izizi zowawa kwambiri

bolo young

๐Ÿ˜ญ๐Ÿ•Š๏ธDear God why ???๐Ÿ’”๐Ÿ˜ญ rest in peace bro๐Ÿ˜ญ๐Ÿ’”
02/07/2026

๐Ÿ˜ญ๐Ÿ•Š๏ธ
Dear God why ???

๐Ÿ’”๐Ÿ˜ญ rest in peace bro๐Ÿ˜ญ๐Ÿ’”

Good morning ๐Ÿ™Or uli offline zifika adimin yambapo aseMama Princess Lifestyle morning
01/07/2026

Good morning ๐Ÿ™

Or uli offline zifika adimin yambapo ase

Mama Princess Lifestyle morning

Address

240 Sherwood Durban
Cape Town
800

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Shaqar the artist posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Shaqar the artist:

Shortcuts

Share