Jesus is coming back soon

Jesus is coming back soon I'm Eunnoch Robert!! I'm a preacher and I repeat the words of God!! ���

Beautiful view 😍
01/02/2026

Beautiful view 😍

Shalom bride of christ 😍
31/01/2026

Shalom bride of christ 😍

03/12/2025
12/11/2025

Mulungu analonjeza kudzakwanilitsa ndipo ingokhupililani iye ndipo matenda anu onse achilitsidwa mu Dzina la YESU KHRISTU Amen 🙏

09/11/2025

Kondani Ena monga momwe Mulungu akukondelani posatenger nyengo zomwe mukudutsa kapena ma udan Ena mu Dzina la Yesu khristu Amen🙏

05/11/2025

Ndikutsutsana ndi satana
Mu Dzina la YESU mwana wa MULUNGU landilani machilitso kwa inu nonse muli mu m'singa zamatenda lero Amen!

Pomwe kunja kwacha moyo wanu nawo ulandile zisomo za tsopano mwa mphamvu ya MULUNGU zichitike pa moyo wanu lero!!
03/11/2025

Pomwe kunja kwacha moyo wanu nawo ulandile zisomo za tsopano mwa mphamvu ya MULUNGU zichitike pa moyo wanu lero!!

03/11/2025

Ambuye akutetenzeleni kwa adani anu mamawa uno mu Dzina la YESU KHRISTU ingolembani kuti Amen 🙏

Address

Vereeniging

Telephone

+27659576178

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Jesus is coming back soon posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share