Nsanje Post

Nsanje Post Your trusted source for Political News Updates and Trending News in Malawi and beyond. [email protected]
(4)

Pa ground pafewa ndi 𝐧𝐠𝐨𝐧𝐠𝐨𝐥𝐞 𝐲𝐚 𝐂𝐃𝐅🤝. Amayi ndi Achinyamata 𝐚𝐭𝐚𝐤𝐚𝐭𝐞!!😁
08/01/2026

Pa ground pafewa ndi 𝐧𝐠𝐨𝐧𝐠𝐨𝐥𝐞 𝐲𝐚 𝐂𝐃𝐅🤝. Amayi ndi Achinyamata 𝐚𝐭𝐚𝐤𝐚𝐭𝐞!!😁

07/31/2026

INTERVIEW SMALL WIFEY in 18+
~Anali munthu odziwa kucheza🥲

  PLANE CRUSHJOHN MSONTHI~anangolosera kuti ndege yagwa ndipo yaphenya mtengo
07/31/2026

PLANE CRUSH
JOHN MSONTHI
~anangolosera kuti ndege yagwa ndipo yaphenya mtengo

  news REST IN PEACE MBUMBA😭~Mmodzi mwa owulutsa mawu ku kanema ndi wailesi ya Times Mbumba Tiyamike Nkhoma wazaka 31 wa...
07/31/2026

news
REST IN PEACE MBUMBA😭
~Mmodzi mwa owulutsa mawu ku kanema ndi wailesi ya Times Mbumba Tiyamike Nkhoma wazaka 31 wamwalira atachita ngozi pa Nyale pafupi ndi pa Mlangeni m'boma la Ntcheu.

Mneneli wapolisi ya Ntcheu a Jacob Khembo atsimikiza izi ndipo ati anthu ena asanu avulala.

07/31/2026

NAMIWA ARRESTED;
Right activist in Malawi got arrested because he uncovered the corrupt ministers in Malawi who has accumulated a lot of worthy within 8 months in Government.

here is the VIDEO

07/31/2026

Leader of Opposition in Parliament CHITHYORA BANDA has rejected the Recognition of President Peter Mutharika as Best president in AFRICA by APAC

  NAMIWA WAMANGIDWA?🤢AMBIRI AKUDWABA ~Mr Namiwa Amkagwira ntchito ndi DPP muzaka za 2014-2019 kenako basi kuyamba kumako...
07/31/2026

NAMIWA WAMANGIDWA?🤢
AMBIRI AKUDWABA
~Mr Namiwa Amkagwira ntchito ndi DPP muzaka za 2014-2019 kenako basi kuyamba kumakokana ndi MCP pano zathekanso bwanji amangidwa ndi Boma lawo la DPP chifukwatu anali ku State house,
👂Angwirapo ku wailesi ya DPP ya FM kumalimbana ndi MCP.

Ulendo uno DPP sikufuna kumacheza ndi anthu anthera kuwiri,
WAMANGIDWA CHIFUKWA CHONYOZA NDUNA ZABOMA
CHIPUNGU & Chisale

ATUPELE MULUZI ON NAMIWA ARREST😳..................................................................................  wa c...
07/31/2026

ATUPELE MULUZI ON NAMIWA ARREST😳..................................................................................
wa chipani cha United Democratic Front (UDF), Atupele Muluzi, wati akuyimira Mtsogoleri wa bungwe la Centre for Democracy and Economic Development Initiatives (CDEDI), Sylvester Namiwa, potsatira kuyitanidwa kwake ndi likuku la Police ku area 30 ku Lilongwe kuti akafunsidwe mafunso.

a Muluzi ati dziko la Malawi likuyenera kuteteza mfundo za kuwonekera poyera, kuyankha pa udindo komanso ufulu wokambirana nkhani za dziko popanda mantha.

PACHICHEWA PALI MAWU: Menya galu kuti udziwe mbuyache

  news UTM PRESIDENT DR KABAMBE WALUSA!!!~chifukwa chomangidwa kwa Sylvester Namiwa (CDEDI LEADER) 😝.......................
07/31/2026

news
UTM PRESIDENT DR KABAMBE WALUSA!!!
~chifukwa chomangidwa kwa Sylvester Namiwa (CDEDI LEADER) 😝.......................................................................................................................................👂NAMIWA wamangidwa dzulo pazifukwa zoti amanyoza ma Minister awiri HON CHIPUNGU ndi HON CHISALE

pachichewa pali mawu>Menya galu kuti udziwe Mbuyache amene amutuma,

07/31/2026

Ritah Mkandawire wapezeka ku Karonga
aliku Lodge kubisala kkkk Malawi akugonabe

Adresse

Quebec
Montreal, QC

Notifications

Soyez le premier à savoir et laissez-nous vous envoyer un courriel lorsque Nsanje Post publie des nouvelles et des promotions. Votre adresse e-mail ne sera pas utilisée à d'autres fins, et vous pouvez vous désabonner à tout moment.

Raccourcis

Partager