The New Flames

The New Flames Genuine Page where latest News are found

11/08/2025

With Gogo Gowoka – I'm on a streak! I've been a top fan for 7 months in a row. 🎉

President Chakwera atsimikizira anthu aku Nthalire zitukoko zosiyanasiyana akawavoteranso.Mtsogoleli wa dziko lino Dr La...
11/08/2025

President Chakwera atsimikizira anthu aku Nthalire zitukoko zosiyanasiyana akawavoteranso.

Mtsogoleli wa dziko lino Dr Lazarus McCarthy Chakwera anati ma Boma a mbuyomu samaganizira anthu aku Nthalire m'boma la Chitipa pa zitukuko zosiyana siyana.

President Chakwera amayakhula izi pa mwambo otsegulira chipatala Cha Nthalire Community chomwe chamangidwa mwa makono mothandizana ndi a Press Trust.

"Ma Boma a m'buyomu samaganizira anthu akuno kuti akufunikira miseu, zipatala kapena amapanga zitukuko kwawo kokha. Anthu aku Nthalire ndi a Malawi ngati mene alili maderanso ena," adatero a Chakwera.

"Mene mudandikhulupirira pa chisakho cha 2019 ndikupephaniso kuti tikadutsa pa 16 September apa ndipitilize zitukuko komwe tayamba kale," adafotokoza.

Yemwe akuimira chipani cha MCP pampando wauphungu mdera la Chitipa South pa chisankho cha pa 16 September pano, Werani Chilenga, anapempha anthu mderali kuti adzavotere President Dr Lazarus Chakwera ndi omwe akuimira chipanichi mmipando ya aphungu ndi makhansala pa chisankho chikudzachi.

A Chilenga anapemphaso boma kuti liganizire zopanga derali kukhala boma palokha.

Poyankhula polandira mtsogoleri wa dziko lino Dr Lazarus Chakwera, Senior Chief Nthalire inali yokhutira ndi boma kamba kokuza chipatala cha Nthalire kukhala chokulirapo, (Community Hospital) ponena kuti Iwo ndi mafumu anzawo agwirizana kuti adzigwira ntchito ndi a Chakwera kuti akadutsa pa 16 September apa apitilize zitukuko zosiyana siyana.

Potsiriza, Senior Chief Nthalire inapempha mtsogoleri wa dziko lino kuti boma lake likonze msewu wochoka ku boma la Chitipa, omwe ndi ma Kilometre okwana 120.

23/07/2025

ORANT CHARITIES IMUKANA KHUMBENI PAMODZI NDI AMBULANCE YAKE; NO TO CASHGATE MONEY

M'modzi mwa omwe akupikisana Ku Dowa Ngara Hon Rodwell Khombeni waona mazangazime chipani chitamukanira ambulance pamodzi ndi ndalama zake.

Iwo akuima payekha.

ORANT yamutsimikizira kuti Iwo Ali ndi Ma ambulance okwanira ndipo sangalandire ina.

Paza ndalama Zomwe Amati apeleke Bungwelo lati Lili ndi ndalama zochuluka ndipo ndizopanda Nzeru kulandira ndalama kwa Shadow yemwe ndalama zake ndiza Cashagte

Tsotsi yemwe amakhala pa Kasese ndiye akusunga ndalama zokanidwazi ndipo wati azichotsapo kuti amalizire nyumba zake zomwe akumanga.

23/07/2025

Mfundo zikulu zikulu zomwe zili mu loko otsegula kuchokera kwa Dr Joyce Banda akatenga dziko lino pa 16 September pano

1. Tizatumiza achinyamata 100,000 ku Dubai kuti akagwile ntchito zosiyanasiyana kumeneko aku Dubai takambilana nawo kale akungodikira kuti tiwine basi.

2. Ife a a PP tagwilizana kuti tizapeleke maphunziro awulere a secondary m'dziko muno chifukwa zomwe zikuchitikazi ndi m'nyozo kwa amphawi kumalipilitsana sukulu

3. Ndiwonetsesa kuti a Malawi tayamba kulimira ma Trakitale khasu izakhala mbiri yakale mu ulamuliro wathu

4. Ndizabwezeletsanso nsomba mu lake Malawi kuti nonse okhala mbali mwa Nyanja muyambilenso kumva kukoma

5. Pofuna kutukula achinyamata ndizapeleka Njinga zakabaza zaulere

23/07/2025

Mlembi wamkulu wa chipani cha Malawi Congress, *Richard Chimwendo Banda,* wati anthu a chigawo cha Kumpoto sangayiwale nkhaza zomwe chipani cha DPP chnawachitira panthawi yomwe chimkalamulira dziko lino, ponena kuti njira yosankhira ophunzira potengera komwe akuchokera, Quota system, pachingerezi inali nkhaza imodzi yomwe inapweteka anthu a Kumpoto mkulepheretsa ana anzeru kupitiliza ndi maphunziro awo.

*Chimwendo Banda* amalankhula izi lachiwiri pa 22 Julayi, 2025 pa bwalo la masewero la Mzimba pomwe Mtsogoleri wa chipani cha Malawi Congress, yemwenso ndi Mtsogoleri wa dziko lino Dr Lazarus Chakwera amakhazikitsa ntchito ya misonkhano yokopa anthu kudzamuvotera chipani cha MCP mchigawo cha Kumpoto.

Chimwendo anati chipani cha Malawi Congress ndichodala pokhala ndi Mtsogoleri wa masomphenya, yemwe akufuna kukweza dziko, mopanda tsankho.

"Tikuthokozeni kuti munavomera kuyimiranso chipani cha Malawi Congress Party, koposaposa kuti mutumikire mtundu wa Malawi. Mwakhala Pulezidenti oyamba kuphunzitsa kuti chitukuko chizifika dziko lonse la Malawi mosakondera" Anatero Mlembi wamkulu wa chipaniyu.

A Chimwendo anatsindika kuti Kumpoto kwayalidwa zitukuko zowoneka ndi maso, monga nyumba yosungira mabuku pa sukulu ya ukachenjede ya Mzuni, mabwalo a masewero a Chitipa ndi Mzimba, maofesi a boma mu mzinda wa Mzuzu, komanso malo ofikira sitima m'boma la Likoma, zomwe anati atsogoleri ena mbuyomu adalephera kamba koti chigawo cha Kumpoto samkachiwerengera.

@ *_Chilimunthaka_*

MAKALA NGOZO REFUTES JOINING UTM!!.. _describes fake stories as "desperation of Lilongwe Mpenu politicians"_ Some undisc...
12/06/2025

MAKALA NGOZO REFUTES JOINING UTM!!
.. _describes fake stories as "desperation of Lilongwe Mpenu politicians"_

Some undisciplined and unprincipled politicians in Lilongwe Mpenu Constituency have resorted to fabrication of stories that Honourable Aaron Makala Ngozo had deflected to the opposition UTM.

Thorough verifications from all reliable sources have proved the news as " _baseless_ " and " _unfounded_ " with many characterizing them as _meaningless politics_ " and " _last kicks of dying horses_ " of the incubent

These stories follow a recent road maintainance initiative that Makala Ngozo took at Nsanjiko in the constituency.

"It is sad to learn that these stories are emerging after I have just maintaned the road. We can do better as politicians. Let us not be too much desperate for power," said Makala Ngozo.

Meanwhile, constituents of Lilongwe Mpenu have collectively reverberated that what they all need is meaningful development in the constituency not witch-hunting politics.

11/06/2025

I got over 50 reactions on my posts last week! Thanks everyone for your support! 🎉

*Drunk Cop Shoots Unarmed Lawyer Over Petty Dispute: Midima Court Slams Police Brutality.*In a shocking revelation, it h...
11/06/2025

*Drunk Cop Shoots Unarmed Lawyer Over Petty Dispute: Midima Court Slams Police Brutality.*

In a shocking revelation, it has been established that the police officer who discharged live ammunition at unarmed lawyer Bob Chimkango was drunk on duty, sparking outrage and raising concerns about law enforcement conduct in Malawi.

According to eyewitnesses cited in the official police report, officers manning the roadblock observed a vehicle approaching with a visibly deflating rear tire. Despite signaling the driver to stop, the car passed the checkpoint and came to a halt just meters beyond. What followed, however, was an abuse of power that nearly turned deadly.

One of the officers, allegedly demanding money, confronted Mr. Chimkango. An argument ensued. The officer reportedly assaulted the lawyer, provoking a defensive reaction in the heat of the moment.

Instead of de-escalating, the officer escalated the situation to a near-execution, firing live rounds at the stationery vehicle, luckily Chimkango was not in the car.

In a rare moment of judicial clarity, the Senior Resident Magistrate’s Court at Midima dismissed the case against Chimkango, ordering only a minor fine of MK15,000 for what it termed an insignificant offense.

In delivering judgment, the court condemned the use of lethal force against civilians, particularly one who grew up in the area and whose parents still reside there.

The presiding magistrate posed a chilling question: “If bonafide members of the community are met with such brutal force for small issues, what fate awaits those who are strangers to the area?”

The court didn’t mince words, warning police against the reckless use of force and stressing that justice will eventually catch up with officers who abuse their power, no matter how long it takes.

It was also established that Chimkango has no gun shot wounds and there was no car chase as earlier reported by the police.

GREAT SON OF NDENDERA DIES One famous and grand father to many in Chakwera Village near Galangombe passed on 28 May. He ...
29/05/2025

GREAT SON OF NDENDERA DIES

One famous and grand father to many in Chakwera Village near Galangombe passed on 28 May. He was well known at Madisi Trading Centre.

He knew history of Dowa having witnessed the coming of Kamuzu Banda at Chileka International Airport in 1957.

Ndendera's son born in 1937 and grew up in M'komba village, Dowa.

You cannot mentioned Madisi without mentioning his Name.

May His Soul Rest in Peace

Mtsogoleri wa dziko lino Dr Lazarus Mccarthy Chakwera wafika munzinda wa Blantyre kudzera pa bwalo la Chileka mu mzinda ...
22/05/2025

Mtsogoleri wa dziko lino Dr Lazarus Mccarthy Chakwera wafika munzinda wa Blantyre kudzera pa bwalo la Chileka mu mzinda wa Blantyre.

Yemwe walandila mtsogoleri wa dziko linoyu ndi nduna yoona za madzi ndi ukhondo yemweso ali wachiwiri kwa wachiwiri ku chipani cha Malawi Congress (MCP) olemekezeka Abida Mia komaso wachiwiri kwa mlembi wa chipani cha MCP olemekezeka a Gerald Kazembe ndi akuluakulu ena aboma komanso achipani.

Dr Chakwera akuyembekezeka kutsegulira chionetsero chamalonda cha nambala 35 ku Trade Fair m'mawa uno mu mzindawu.

BOMA LA KONGERESI LALEPHERA
27/04/2025

BOMA LA KONGERESI LALEPHERA

Adresse

Democratic Republic Of The

Notifications

Soyez le premier à savoir et laissez-nous vous envoyer un courriel lorsque The New Flames publie des nouvelles et des promotions. Votre adresse e-mail ne sera pas utilisée à d'autres fins, et vous pouvez vous désabonner à tout moment.

Contacter L'entreprise

Envoyer un message Ă  The New Flames:

Partager