04/08/2026
Mawa tikuyamba 🔥
Kodi munaphunzirapo kusukulu kuti Kamuzu Banda anali ndani kwenikweni?
"Ngwazi" basi. Kapena "Wachiwawa" basi.
Nkhani yeniyeni ndi yovuta kuposa imeneyo.
Kuyambira mawa pa "THE LINO ARCHIVE" tikuphunzitsa mbiri ya Malawi yomwe simunaphunzitsidwe m'kalasi.
HERO KAPENA WACHIWA? - Dr. Kamuzu Banda
Follow tsopano kuti zisakuphonyeni ??
HISTORY Facebook for Creators Following Teachers Pay Teachers Facebook Teaching