21/08/2025
ποΈβ¨ Stee OnTheBeat β Home Recording Studio
Kodi muli ndi nyimbo koma mulibe malo oti mulembere?
Bwerani ku studio yathu ku Sochi!
Ifenso tilipo kukuthandizani:
β
Recording
β
Mixing
β
Mastering
π₯ Timapanga nyimbo yanu iumveke pro mosavuta komanso pa mtengo wabwino.
π Location: Sochi
βοΈ 0994653162 / 0899500898
π© DM or Call to Book Your Session