Vital Talks with AlyHill

Vital Talks with AlyHill REGISTERED NURSE🩺 ||QUEEN 👸||EDUCATOR 🇲🇼🇿🇦🇬🇧
Real talks as the spirit leads
I run solo Podcast
Sharing daily dose of wisdom😇
(2)

01/09/2026

Kodi pa fesibhukhu ungapezepo mamuna wa siliyasi mpaka banja ndithu? Akufunsa kuseliku

01/09/2026

Kodi ndizoyenela kuti mamuna azimuthandiza mkazi wake ntchito zapakhomo monga kukolopa, kuchapa, kutsuka mbale…?

01/09/2026

Azimai
Kodi nchani chimene chimapangitsa kuti interest yanu ithe pa mamuna wanu? Kufika pomati what was I thinking kuwavomela awa?

Azibambo kumastand….men shut it the ladies are talking

31/08/2026

Azibambo
Kodi chani chimapangitsa kuti nzimai kapena ndinene kuti mkazi wanu asiye kukuonekelani okongola?

Azimai kumastand….Ladies shut it men are talking

MoniKuno magobo anakaka moti apa kutuluka kumeneNdakusowani🤭
30/08/2026

Moni
Kuno magobo anakaka moti apa kutuluka kumene
Ndakusowani🤭

29/08/2026

Pamene tili mu nyengo ya AI pqchizungu nditi tchatijipiti. Make I beg una 🙏🙏 do not ask AI the things of God. Don’t ask AI to interpret scripture for you. Ngati simukumvetsetsa ask the Holy Spirit. Thats His job teaching you and revealing those deep mysteries hidden in the word. M***a ku mafunsa mafuso ena ndi enawa but when it comes to scripture musiyireni mwini wake mzimu oyera akuululireni. Do not quench Him
It’s sad you see a post from a whole man of God tchatjipiti language written allover it akuti interpreting scripture. Agalatiya wakulodzani ndani?🥺🥺
Good morning

28/08/2026

Akufungatileni yahweh
🙏🙏🙏

28/08/2026

I have a khweshin. As a married woman. Chithunzi cha apulofiti chikutani pa profile panu? Osaika hubby iyayi
Auntie why na?!

Masiku awiri apitawa Ndapanga ma levels 3 omwe mamuna amadutsamo. Funso kupita kwa ma ladies ali pa mudzi pano a bae anu...
28/08/2026

Masiku awiri apitawa Ndapanga ma levels 3 omwe mamuna amadutsamo. Funso kupita kwa ma ladies ali pa mudzi pano a bae anu ali level iti?
Nanga Anyamata muli pano mkazi yemwe wapanga emerge into wife mwakumana nae kapena mudakasakambe?
Marriage is a long time osathamangirako … infact make I tell you this maombedwe mmanja akubanja it’s a responsibility ! E no be beans ooo!!!

28/08/2026

You have chopped life size kukana. Gauge ikuoneka chonchi 🕧
But you want marry a viligo. Are you oke?
Sir the thunder that will strike you is still dancing shakara 🤭🤭

Address

London Bridge
London
SE1 9BG

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Vital Talks with AlyHill posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share