VOMI News 247

VOMI News 247 VOMI News 247 is Malawi's leading social media platform and Television station based in Dublin Ireland

China records seven thousand cases of Chikungunya Virus.Musayiwale Lobola kaya mumati Ebola inachokelanso Mandela omwe w...
05/08/2025

China records seven thousand cases of Chikungunya Virus.

Musayiwale Lobola kaya mumati Ebola inachokelanso Mandela omwe wa awa

Koma Onjezani Kenani akuwugeya mwano ndi ma Visa Bond atchukawa.Osafuna USA asale akumvere fungo
05/08/2025

Koma Onjezani Kenani akuwugeya mwano ndi ma Visa Bond atchukawa.

Osafuna USA asale akumvere fungo

UTM Party presidential running mate, Dr. Mathews Mtumbuka, says the party will launch a Business Process Outsourcing (BP...
05/08/2025

UTM Party presidential running mate, Dr. Mathews Mtumbuka, says the party will launch a Business Process Outsourcing (BPO) initiative which is worthwhile for the youth.

According to Dr Mtumbuka , the program will enable Malawian youth to work remotely for international companies, earning up to at least MK 200,000 per day.

The BPO model empowers youth to access digital jobs while staying in Malawi.

Nyumba ya Malamulo yavomereza Lamulo Latsopano la zisankho za mtsogoleriwa dziko, aphungu ndi ma khansala.Izi zikutantha...
05/08/2025

Nyumba ya Malamulo yavomereza Lamulo Latsopano la zisankho za mtsogoleriwa dziko, aphungu ndi ma khansala.

Izi zikutanthauza kuti ogwira ntchito pa zisankho, apolisi ndi oimira anthu kapena zipani za ndale aloledwa kuvotera pa malo omwe adzagwire ntchito pa tsiku la chisankho.

Dziko la Malawi likuyembekezeka kuchititsq zisankho zapatatu pa 16 September.

Malawi's Ntopwa FC have been drawn in Group A of CAF's Women's Championship League qualifiers.This is according to a dra...
05/08/2025

Malawi's Ntopwa FC have been drawn in Group A of CAF's Women's Championship League qualifiers.

This is according to a draw for the competition that took place earlier on Tuesday.

The team will face South Africa's Mamelodi Sundowns, Beauties FC of Namibia and Zesco Ndola Girls FC of Zambia.

The 2025 CAF Women's Champions League| COSAFA Qualifier will take place in Johannesburg from August 22-31, 2025.

Six people have died,  and others are seriously injured following a road accident that happened near Mzimba bridge along...
05/08/2025

Six people have died, and others are seriously injured following a road accident that happened near Mzimba bridge along the Mzupppzu - Jenda M1 road last night.

According to Mzimba police spokesperso Maria Banda, the accident happened after the driver of a DPX Scania fuel tanker going to Lilongwe attempted to overtake another truck and collided with an on-coming Toyota Sienta vehicle.

Banda said the six, whose particulars are not yet know, died on the spot, while the injured ones were rushed to Mzimba district hospital for treatment.

Just InMlangizi wa Chakwera a Martha Kwataine atuluka chipani cha MCP lero.Iwo ati sakufuna akhale kuchipani komwe kulib...
05/08/2025

Just In
Mlangizi wa Chakwera a Martha Kwataine atuluka chipani cha MCP lero.

Iwo ati sakufuna akhale kuchipani komwe kulibe tsogolo komanso chikugwa muboma.

Kodi Democratic Progressive Party - DPP ikunena zowona apa?
05/08/2025

Kodi Democratic Progressive Party - DPP ikunena zowona apa?

05/08/2025

Petulant wasowa ndi nyimbo yomwe mbali yotsutsa boma ikuyimba mu nyumba ya malamuro pakadali pano

Zambiri zikukambidwa za Jappie Mhango Vice President of the Democratic Progressive Party DPP in the North.Apa tikuyesa k...
05/08/2025

Zambiri zikukambidwa za Jappie Mhango Vice President of the Democratic Progressive Party DPP in the North.

Apa tikuyesa kufuna kulankhula ndi m'neneri wa chipani chi ndipo tikupatsirani zambiri.

Nkhani yomwe ikumveka ndiyokuti iye sakufuna utsogoleri omwe ulipo mchipanichi - but this is an allegation.

Titsimikiza

Munamva chani za Maheu ndi Ndale?
05/08/2025

Munamva chani za Maheu ndi Ndale?

04/08/2025

Trending now:

Special advisor on climate change😅

Address

24 Belvedere Place Flat 1, Phibsboro, Dublin 7
Mountjoy

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when VOMI News 247 posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to VOMI News 247:

Share