Baibulo Langa Moyo Wanga TV

Baibulo  Langa  Moyo  Wanga TV Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Baibulo Langa Moyo Wanga TV, TV Channel, East Jerusalem.
(4)

Buku Lopatulika
📓📓📕📔📒📝
kwawo kwa Ulaliki📚

Gospel Music promoters
Gospel of God Adverts
Preachings
For more Information contact
Media Team at👇
+265996020480/+265885421436
[email protected]

13/05/2026

Yeremiya 29:11 CCL

Pakuti Ine ndikudziwa zimene ndinakukonzerani,” akutero Yehova, “ndimalingalira zabwino zokhazokha za inu osati zoyipa, ayi. Ndimalingalira zinthu zokupatsani chiyembekezo chenicheni pa za mʼtsogolo.

13/05/2026

Usiku wa wabwino osaiwala kupemphera 🙏

13/05/2026

Nkhani zake zovuta 🖐️

13/05/2026

Zilikotu ma churchemu

Akanafuna a Yesu akanakana, komabe analolabe kudutsa muzowawazi, ananyozedwa ndipo anava ululu monga angavele munthu ali...
13/05/2026

Akanafuna a Yesu akanakana, komabe analolabe kudutsa muzowawazi, ananyozedwa ndipo anava ululu monga angavele munthu aliyese. Zonsezi anapanga chifukwa chachikondi chake chozama pa moyo wanthu. Anafunitsitsa kuti ayigonjetse infa komaso oyipayo.
Mwazi wa yesu umachiza, mwaziyu umatiteteza, ndipo umatimenyelaso nkhondo zosiyana siyana.
Chivumbulutso 12:11
Abale athuwo anamugonjetsa ndi magazi a Mwana Wankhosa ndiponso mawu a umboni wawo. Iwo anadzipereka kwathunthu, moti sanakonde miyoyo yawo.)

13/05/2026

Vuto Lakolo mayankho Ali ndi Yehomva🙌Mupemphe iye ndipo chizapasidwa Kwa iwe🙏

13/05/2026

Tiyambe ndi Mawu awa

12/05/2026

Ahebri 9:27-28 CCL

[27] Popeza kunayikika kwa munthu kufa kamodzi ndipo kenaka kuweruzidwa, [28] momwemonso Khristu anadzipereka nsembe kamodzi kokha kuchotsa machimo a anthu ambiri. Ndipo Iye adzaonekanso kachiwiri, osati kudzachotsa tchimo, koma kudzapereka chipulumutso kwa amene akumudikira.

12/05/2026

Yehova salakwitsa

A'bale anga, kodi munalandila yesu kukhala mbuye ndi mpulumutsi wanu ?Ngati sitinatelo tiyene tisachedwe. Yesu kristu, n...
12/05/2026

A'bale anga, kodi munalandila yesu kukhala mbuye ndi mpulumutsi wanu ?
Ngati sitinatelo tiyene tisachedwe. Yesu kristu, ndi njila, choonadi, ndi moyo, palibe angafike kwa atate popanda iye.💯❤️

11/05/2026

Chivumbulutso 21:4
[4] ‘Mulungu adzapukuta misozi yonse mʼmaso mwawo. Sikudzakhalanso imfa kapena kukhuza maliro kapena kulira kapena ululu popeza zakale zapita.’ ”

Address

East Jerusalem
EH530EZ

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Baibulo Langa Moyo Wanga TV posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Baibulo Langa Moyo Wanga TV:

Shortcuts

Share

Category