Balaka News Agency

Balaka News Agency Bringing news to your home, were blk news agency just follow us whatever happens in blk you will get to know it ASAP with us
(1)

Happy Birthday πŸŽ‚ Steve MBalaka News Agency
06/06/2026

Happy Birthday πŸŽ‚ Steve M

Balaka News Agency

BALAKA KODI MUKUDZIWA?Anthu okhala ku Balaka komaso madera ena ozungulila dziwani za Chipatala cha Ngwangwa Pvt Clinic.C...
06/06/2026

BALAKA KODI MUKUDZIWA?

Anthu okhala ku Balaka komaso madera ena ozungulila dziwani za Chipatala cha Ngwangwa Pvt Clinic.Chipatalachi chikupezeka pafupi ndi fueling station ya Mount Meru yomwe ili pa Ngwangwa.

A Ngwangwa Pvt Clinic amathandiza matenda osiyana siyana monga odwala osagonekedwa M'chipatala (OPD),Chipatala cha amayi,m'dulidwe ,njira zakulera zamakono,kuyeza khansa yakhomo yachibelekero ndi chipatala cha ana ochepela zaka zisanu komaso matenda ena osiyana siyana.

Masiku otsegula
-Lolemba -Lamulungu
Nthawi yogwirila ntchito -24 Hours

mukafuna kumva zambiri imbani pa ma nambala awa komanso mukhoza kupanga LIKE tsamba lawo la Facebook .

Link below

0881927108
0982577654

powered by Ngwangwa Pvt Clinic πŸ’ŠπŸ’‰πŸ©Ί

Balaka News Agency

Happy Birthday πŸŽ‚ Yankho James Balaka News Agency
06/06/2026

Happy Birthday πŸŽ‚ Yankho James

Balaka News Agency

NKHANI ZA MASEWERA ⚽MARK FODYA JR WAPELEKA JERSEY KU MAPHUNZIRO ACADEMY KOMASO VILLA FC.Katswiri okakha chikopa wakwathu...
04/06/2026

NKHANI ZA MASEWERA ⚽

MARK FODYA JR WAPELEKA JERSEY KU MAPHUNZIRO ACADEMY KOMASO VILLA FC.

Katswiri okakha chikopa wakwathu kuno ku Balaka Mark Fodya Jr yemwe pano akusewela timu ya Manica Diamonds Fc ya dziko la Zimbabwe wapeleka ma jersey osewelera mpira wamiyendo kwa matimu awili omwe ndi Maphunziro Academy komaso timu ya Villa Fc.

Fodya yemwe anasewelapo timu ya Maphunziro Academy thawi yomwe amasewela kuno ku Balaka wapeleka jersey ku timuyi ngat njila imodzi yofuna kulimbikitsa osewela omwe akusewela ku timuyi kuti azichita bwino.Fodya wapelekaso jersey ku timu ya Villa Fc ngati njila imodzi yofuna kupititsa masewela ampira patsogolo m'dziko muno.

Mark Fodya wakhalaso akuchititsa mipikisano ya mpira wa achichepele kuno ku Balaka kwa zaka zingapo. Fodya anasewelapo matimu ena monga Wizard Fc, Silver Striker's asanapite m'dziko la Zimbabwe.

Zabwino zonse mwana wa mmudzi.

Powered by Ngwangwa Pvt clinic πŸ’ŠπŸ’‰πŸ©Ί

Balaka News Agency

Katswiri oyimba chamba cha hip hop kwathu kuno ku Balaka Eminet Wadongosolo watulutsa nyimbo yake yatsopano yomwe ikutch...
03/06/2026

Katswiri oyimba chamba cha hip hop kwathu kuno ku Balaka Eminet Wadongosolo watulutsa nyimbo yake yatsopano yomwe ikutchedwa kuti Amen.

Nyimbo yatsopanoyi Eminet waimba ndi Wangata ndipo yemwe wajambula nyimboyi ndi Tacktic ndi Bannie ndipo yemwe wavokela nyimboyi ndi Tropix Nyimbo. Nyimbo ya Amen yatuluka yomvela komaso ndi ya kanema.

Kanema wa nyimboyi akupezeka pa YouTube ndipo link yake ili mu comment section πŸ‘‡πŸΎ

powered by Ngwangwa pvt clinic πŸ’‰?Balaka News Agencygency

Happy Birthday πŸŽ‚ Elton KasinjaBalaka News Agency
02/06/2026

Happy Birthday πŸŽ‚ Elton Kasinja

Balaka News Agency

NKHANI YA CHISONI πŸ’”πŸ˜­Kucha kwa lero m'boma la Balaka tazizidwa ndi chison pamene mmodzi mwa achinyamata Annastanzia Makum...
31/05/2026

NKHANI YA CHISONI πŸ’”πŸ˜­

Kucha kwa lero m'boma la Balaka tazizidwa ndi chison pamene mmodzi mwa achinyamata Annastanzia Makumbi watisiya.
M'bale wathuyu amakhala ku Andiamo (Lingala) ndipo wamwalira kucha kwa lero pa 31 may.

Anastanzia wamwalilira kuchipatala kwa Mponda komwe anagonekedwa kwamasiku ochepa chabe koma chomwe amadwala kwenikweni sichinaziwike bwino.

Madongosolo onse a komwe ataike komaso tsiku loika mmanda tsikana wathu Anastasia sizinaziwike bwinobwino kuchokera kumtundu koma zikadziwika tibweraso kuzanena.

Mulungu samuchotsa munthu pamalo asanamukomzere pokhala πŸ’” 😭

Rest in peace Anna πŸ•ŠοΈBalaka News Agency Agency

30/05/2026

Big shout out to our newest top fans! S Thu Balaka, Beatrice Bude Humbar, Emmanuel Sekeya, Pempho Ngozo Muntoza, Chixo Wa Hassie, Martha Bunaya Kaumphawi, Hendrina Hassam, Ι­Ι­ ØsikwΓͺ Ι­Ι­, Rensino Malatah

Happy Birthday πŸŽ‚ Griven Comrade MwaluwasaBalaka News Agency
30/05/2026

Happy Birthday πŸŽ‚ Griven Comrade Mwaluwasa

Balaka News Agency

Happy Birthday πŸŽ‚ Samuel Kanyama KhwiyaBalaka News Agency
30/05/2026

Happy Birthday πŸŽ‚ Samuel Kanyama Khwiya

Balaka News Agency

Address

Balaka

Telephone

+265888063063

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Balaka News Agency posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share