11/09/2025
Funso: Za Tonde Wadula tiiwale tsopano?
Yankho: AYI
KUFOTOKOZERA;
Pomwe tikutsendera ku Zisankho, zikumavuta kuti pa KANEMA awonetse Sewero chifukwa choti ma Program Ambiri akumakhala a ndale.
Pomwe tokuyankhulamu, pa YouTube Channel yathu tawonetsa ma Episode ochulukirako kuyelekeza ndi pa TV.
Tipepetse kuti sizinathe kukupatsani Update imeneyi mu nthawi yoyenera, koma tangopuma sabata imodzi yokha ndi cholinga choti tigwirane ndi pa TV.
Ambuye akudalitseni.