09/03/2024
Unduna woona za madzi ndi ukhondo ukuchenjeza tonse kumwera kuno kuti tikhale osamala chifukwa pali chiopsezo kuti mitsinje ina itha kusefukira chifukwa cha mvula ya mphamvu yomwe iyambe mawa pa 10 March 2024.
Chenjezeroli abale anga likupita kwa tonse akuno ku mwera , silikusankha dera kapena malo. Kulibwino kuzitenga kuti tili pachiopsezo nkuzapeza kuti sitinali pachiopsezo kusiyana ndikuzitenga kuti sitili pachiopsezo nkuzapezeka pachiopsezo chovuta Kwambiri.
The Ministry of Water and Sanitation informs all of us in the southern region that there is a risk of floods along some rivers in the the region because of a tropical storm that starts tomorrow the 10th of March 2024.
This cautionary message is for all of us in the region, no area or district is exceptional. It’s better to consider ourselves at risk and realize later that we weren’t, than to think that we are not at risk when we are actually in the path of danger.
Be safe. ❤️
Ministry Of Water and Sanitation - Malawi
Adecots Malawi
UNICEF Malawi