
16/06/2025
Mzanga wachamba chachabe chophwanywa cha dancehall watulutsa kanema wake uyuu okoma zedi🔥 ngati simukhulupirir tiyeni tonse Ku YouTube channel yake tikazionere tokha ndipo tiyeni tim'chite support mfanayu.
N Focus Focus hustle.
https://youtu.be/p5qoCcx7ay4?si=YHTcvK9vj_4Xr5ST
Watch it and you'll thank me later🙏