OSAKA Nasheed PRO

OSAKA Nasheed PRO Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from OSAKA Nasheed PRO, Digital creator, Blantyre.

Bwalo lalikulu loweruza milandu  mawa pa 25 November 2025 likuyembekezeka  kumva ngati kuli nkoyenera kupereka chiletso ...
24/11/2025

Bwalo lalikulu loweruza milandu mawa pa 25 November 2025 likuyembekezeka kumva ngati kuli nkoyenera kupereka chiletso choletsa mzikiti wa Kachanga ku chileka m'boma la Blantyre kupanga adhan.

Sukulu ya Kalibu academy ndi yomwe inapempha chiletsocho ponena k*ti kuyitanira anthu ku mapempheroko kukumadzetsa mphokoso lomwe likumasokoneza ntchito ya maphunziro pa sukulupo.

Oweruza milandu Justice Tembo ndi yemwe amvelere mlanduwu.

16/10/2025

assalaam alykm warhamatullah wabarakatuh
followers

 #1. Nde chi abayacho chiguduli tu munthu kubvala abaya ngat wabisala mu carpetπŸ™„πŸ™„πŸ™„ #2.  muslim girls lets be honestTitat...
13/09/2025

#1. Nde chi abayacho chiguduli tu munthu kubvala abaya ngat wabisala mu carpetπŸ™„πŸ™„πŸ™„
#2. muslim girls lets be honest
Titat takupatsan 1650 pa sula iliyose munaloweza nde k*t muonjezera zingat k*t mukagule abaya?

#3. Abaya ngati raincoat 🀣🀣🀣🀣🀣Chi umbrella tu ati atamangira lamba wake phaaa! Ndendende!! Mtolo wa mzimbe ine ndimafuna tu kukhala Chete koma ayi pepani🀣🀣🀣🀣🀣inu muzibvala ma dress aja mumakongola

#4. Ndavomeleza
Abaya ndigula
Koma everyday pogona
Uziwerenga Quran
First page up to the last one.

#5. Munthu umatopa ndikusoka ma abaya

ma itel users mutionesa zinthutunchani ichi mwezi omwewu
07/09/2025

ma itel users mutionesa zinthutu
nchani ichi mwezi omwewu

πŸ’₯πŸ’₯πŸ’₯πŸ’₯πŸ’₯NAMIBIA πŸ‡³πŸ‡¦ 1-2 FLAMES πŸ”₯ πŸ‡²πŸ‡Ό
05/09/2025

πŸ’₯πŸ’₯πŸ’₯πŸ’₯πŸ’₯

NAMIBIA πŸ‡³πŸ‡¦ 1-2 FLAMES πŸ”₯ πŸ‡²πŸ‡Ό

inu inu kumakhalako achangu pofuna kupeza zinthu zabwino Osamakhala otsalira ayichimbale cha  Ndi   mumvera CHIMBALE CHA...
01/09/2025

inu inu kumakhalako achangu pofuna kupeza zinthu zabwino Osamakhala otsalira ayi
chimbale cha
Ndi
mumvera CHIMBALE CHA MALINGIZO

Yakin YK Hussein

 Yakin YK Hussein ichichi tichimvela lero 5 thousand kwacha kodi ayse ukungotayisa bwanj?
01/09/2025


Yakin YK Hussein
ichichi tichimvela lero
5 thousand kwacha kodi ayse ukungotayisa bwanj?

achina Rashid J Rashy Bashir Poet Kinanah JannahMuhsin AlisenRashid Bashir nthawi iyiyi ma guy awaasakudziwa angakhale b...
31/08/2025

achina Rashid J Rashy Bashir Poet Kinanah Jannah
Muhsin Alisen
Rashid Bashir
nthawi iyiyi
ma guy awa
asakudziwa angakhale button lothimitsira phone
pano ak*tulutsa chi album mbambande

Komatu achina Rashid J Rashy BashirNdi azizanu simukucheza bwino wayambisa ndani izi πŸ˜…πŸ˜…πŸ˜‚πŸ˜‚
31/08/2025

Komatu achina Rashid J Rashy Bashir
Ndi azizanu simukucheza bwino wayambisa ndani izi πŸ˜…πŸ˜…πŸ˜‚πŸ˜‚

Address

Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when OSAKA Nasheed PRO posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to OSAKA Nasheed PRO:

Share