Chayil Multimedia Malawi

Chayil Multimedia Malawi CMM is Malawi's Fastest Growing Online Advertising Brand 🇲🇼
(7)

13/07/2026

"I am a holder of a degree in Surprise & Appreciation Studies obtained from Max & Sherry Institute of Surprises!" Interviewer 🤯

Basi tingoti aliyense ndi dolo pa zomwe amapanga. Nkhaniyi ithe tsopano. Chris Loka wapeza ma customers ndi ma followers...
13/07/2026

Basi tingoti aliyense ndi dolo pa zomwe amapanga. Nkhaniyi ithe tsopano. Chris Loka wapeza ma customers ndi ma followers, Max and Sherry yapeza ma students.

13/07/2026

Zinthu zija zimafunika kuyamba pang'onopang'ono kenaka kumaliza mwamphamvu! Osangofikira pa chorus. Record imakandikatu anzanga!

Azimayi pano anachangamukatu, zopusa sakupanga nawo.Gentlemen m***a kukhala mu chibwenzi chosagonana popanda kuwiringura...
13/07/2026

Azimayi pano anachangamukatu, zopusa sakupanga nawo.
Gentlemen m***a kukhala mu chibwenzi chosagonana popanda kuwiringura, kumangocheza ndi kumenya ti ma cuddles apo ndi apo?

Inuyo kaziyimbani zitini ndi supuni, ife tiziyimba zitoliro zathuzi mwamva?
13/07/2026

Inuyo kaziyimbani zitini ndi supuni, ife tiziyimba zitoliro zathuzi mwamva?

MA PLAN ONSE MU BAJETI ASEMPHA NSEUPatangotha miyezi itatu atapereka bajeti, akuti zonse zimene anapenekera zasinthiratu...
13/07/2026

MA PLAN ONSE MU BAJETI ASEMPHA NSEU

Patangotha miyezi itatu atapereka bajeti, akuti zonse zimene anapenekera zasinthiratu. Sizili m'mene amaganizira.

Zinthu izi zasempha nseu;

1. Kukula kwa chuma. Iwo amati chikwera ndi 4.1%, koma World Bank yatsitsa kufika pa 2.1%.

2. Kakweredwe ka mitengo ya zinthu amati kakhala kosaposa 15% koma pano kali pa 21%.

3. Kupelewera kwa ndalama zimene boma limafuna kugwiritsa ntchito kukupitilira pamene zofuna ndi zimene akutolera zikusiyana.

Zonse akuti zikusiyana ndizimene anaika mu bajeti.

Zonsezi patangotha miyezi itatu yokha.

Ndipo komiti ya Budget and Finance ku parliament ikuti bwanji apangenso mwina zigwirizane ndi zimene zili pa ground.

------------------------------------

Yatero nyuzipepalayi yaleroyi. Mwachidule.

~ Chawezi Banda

Komatu ukuku fans nde ikutokota eh!Basitu Chris Loka watenga zinthuzi! 😅
12/07/2026

Komatu ukuku fans nde ikutokota eh!
Basitu Chris Loka watenga zinthuzi!
😅

Applications are now open :- Max & Sherry yatsegula ma class ophunzitsa anthu zama Surprises & Appreciation in a creative way. It will be open to 10 participants where they will have a 3 day free training sponsored by their partners🥳🥳🥳

Applications are now open

12/07/2026

Masiku ano anthu
1. Sakuwopa HIV
2. Sakuwopa Mimba
3. Sakuwopa Mulungu

Anajomba Ku church ndi kukoka lehu, koma si zomwe akumana nazotu!
12/07/2026

Anajomba Ku church ndi kukoka lehu, koma si zomwe akumana nazotu!

12/07/2026

Ladies tiyeni tibvale modzilemekeza pamene tikupita ku church. Osayanika za mkati kuwopa kugwetsa Mtumiki wa Yehova! Tikumvana?

Address

Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Chayil Multimedia Malawi posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Chayil Multimedia Malawi:

Shortcuts

Share