20/09/2025
ZIZINDIKILO 9 ZIMENE MUDZADZIWE KUTI ASATANIC KAPENA AFITI ANAKUGWILANI PA MOYO WANU
NDIPO AKUUSEWELESA
1,kumakhalila moyo okhumudwa ,kukwiya kwiya
=muthu opephela okondedwa sumayenela kumakhalila kumakhumudwa ndi zozizila zomwe ayi
2,kusapita chitsogolo mu zithu zanu
=dziwani kuti afiti ndi ASATANIC ndi maukulu oyipa amene sasangalala muthu akamapita chitsogolo koma kubwelela mmbuyo ,moti ngati zithu zanu sizikusitha
=kaya banja lanu kaya business yanu kaya tchito chigwilileni koma popanda chochita ayi alipo adakupondelezani
3,kumakhalila kulota joka,,nyau,,kugonedwa,,kulephela kuwoloka mtsinje kulephela kukwela phili,,kumadyesedwa kutulo kulota mzungu,,kulota mkango,kulota milamba ndi zina zotelo dziwani kuti alipo ASATANIC kapena afiti anagwila moyo wanu
4,makhalila kukumana ndi matsoka pa moyo wanu mwina gogole pa moyo ,Anthu kuwabweleka ndalaama koma osakupasa, zimakhala kuti satana akugwila moyo wako
5,kumakhalila kudedwa pa zifukwa zoti zosakwanila komaso kusakondeledwa pa malo
6,kufooka mu umoyo wa pephelo pa moyo wako ,kumakhalila pa phoni 6 to 6 pa phoni njala yose yamau AMULUNGU osamawafuna ayi
7,kumakhalila muthu KUBUNYULA akazi ndi amuna ena mwa Anthu mumakonda kunena kuti ine nde banja ayi ,mudziwa kuti mukufuna kuti muzikhalila kumabunyula
8,akazi wako kapena mwamuna wako sumakhala naye ndi chilakolako koma mkazi wakunja kapena mwamuna wakunja ,ichi ndi chizindikilo kuti pa iweyo ziwanda zasatana zikujoyapo pa moyo wako
9,kusakhala ndi moyo osavomekeza nyengo zimene ukudusamo komaso kusafuna kuphuzitsidwa liuma kapena thota ,,ana asatana safuna kutsutsidwa koma kaka pa zithu zoti alibe nazo umboni
KUTI MUTULUKEMO PANGANI IZI
1acolit 3v16 akuti kodi simudziwa kuti muli kachisi wa MULUNGU ndipo mzimu woyela agonela mwa inuyo??
aheber 12v29 MULUNGU ndiye moto onyekesa
dziwani kuti pamene pamaphikidwa nyama ,,kuti nyama inja muyike pa moto or galuyo atakhala wamisala koma chapamoto sachikhudza
Ziwani kuti ngati mungakhazikike pamaso pa Mulungu M'choonadi Mulungu adzaika moto pa inu ndipo satana sadzakufikirani
Aheberi 12:29
Satana amapita pomwe palibe moto wa Mulungu
AMBUYE AKUDALITSENI NONSE π
AMEN