TRUTH MEDIA

TRUTH MEDIA This is the only Official Page of Prophet Oswald Chizala founder and president of Light of Truth International Ministries.
(1)

Mulungu amene anakulitsa malire a Yabesi akulitsenso malire ako leroli.Mulungu amene anabereketsa nkhalamba Sarah akuber...
14/05/2026

Mulungu amene anakulitsa malire a Yabesi akulitsenso malire ako leroli.

Mulungu amene anabereketsa nkhalamba Sarah akubereketsemso iweyo leroli

Mulungu amene anamutola Davide k*thengo ndikumukwedza kukhala Mfumu, ak*tolenso iweyo ndikukukwedza.

Mulungu amene anasintha Chigawenga Paulo kukhala Mtumiki wake wa Mphamvu asinthenso azibale ako, Amuna ako, Mkazi wako, Mwana wovuta uja.

Mulungu amene alibe sankho achite ndi moyo wako leroli

Mdzina la Yesu Khristu

AMEN

NGATI MUKUFUNA PEMPHERO LAPADERA KOMASO KUMASULIRA MALOTO KAPENA KULANDIRA YESU KHRISTU KUKHALA MBUYE NDI MPULUMUTSI WA MOYO WANU

TILANKHULENI PA👇

WHATSAP OR CALL
(+265) 992 275 595

HALLELUJAH🙏

12/05/2026

*ZOMWE ZIMATCHINGA MAYANKHO POPEMPHERA
✍️✍️✍️

1 ATESALONIKA 5 :17

1.UCHIMO✍️✍️✍️

YESAYA 59:1-2

➡️Pamene pali uchimo Maka kuchimwira dala, osamvera Mau a Mulungu, Mulungu sangamve pemphero lako.

➡️Ndipo sulandira kukonderedwa kwa Mulungu pamoyo wako.

2.MANTHA✍️✍️✍️

2 TIMOTEYO 1:7

➡️Mantha amachokera kwa satana.

➡️Mantha amakuchotsera chikhulupiliro.

➡️Mantha ndiowopsa pak*ti amak*talikitsa ndi Mphamvu ya Mulungu.

➡️Mantha amakuchotsera chiyembekedzo.

➡️Ngati mukufuna mayankho ku pemphero lanu osaopa nyengo yomwe mukuipemphelerayo.

➡️Nyengo izikhala pansi Mulungu pamwamba pa nyengo.

3.KUDZIYIMBA MULANDU✍️✍️✍️

➡️Tingoyetselera ukupemphera koma ukukumbukira zolakwa ndi machimo omwe wachita kapena unachita.

➡️Kudziyimba mulandu ndi vuto lalikuru pakati pa Akhristu ambiri.

➡️Mulungu akakhululuka sakumbukiramso ndie osamadziyimba mulandu popemphera Mulungu anakhululuka kunatha.

➡️Kudziyimba mulandu kumatchinga mayankho kumapemphero athu.

4.KUDZIKAIKIRA PAMASO PA MULUNGU✍️✍️✍️

➡️Anthu ambiri amadzimva kuperelewera pamaso pa Mulungu.

➡️Kudzitenga k*ti pemphero lawo silokwanira pamaso pa Mulungu ndipo izi ZIMATCHINGA mayankho.

5.KUSAKHULUPILIRA✍️✍️✍️

AHEBERI 11:6

➡️Opanda chikhulupiliro sitingamusangalatse Mulungu.

➡️Pemphero lopanda chikhulupiliro siliyankhidwa.

NGATI MUKUFUNA PEMPHERO LAPADERA KOMASO KUMASULIRA MALOTO KAPENA KULANDIRA YESU KHRISTU KUKHALA MBUYE NDI MPULUMUTSI WA MOYO WANU

TILANKHULENI PA👇
WHATSAP OR CALL
(+265) 992 275 595

HALLELUJAH🙏

08/05/2026

TAMVETSERA MWANA WA MULUNGU
✍️✍️✍️

SALIMO 35
YESAYA 54:17

Ngati unaneneredwa uneneri koma sukukwaniritsidwa osadandaula ngati ali Mulungu amene analankhula ukwaniritsidwa.

Kuyambira lero chirichonse chomwe ungachite chizipambana.

Mulungu asusane ndi kulimbana ndi adani ako onse.

Palibe chida chosulidwira moyo wako chomwe chidzapambane.

Mulungu abwedzeretse banja lako ntchito yako komaso chuma chako.

Aliyense amene adakuiwala akukumbukire leroli ndikuyamba kuk*thandidza.

Onse okuwukira awone polekera leroli pak*ti Mulungu ali mbali yako.

Matembelero ndi maguwa aku mtundu leroli awonongedwe.

Mulungu akuchiritse ku nthenda zonse zomwe zimakusautsa.

Mdzina la Yesu Khristu

AMEN

NGATI MUKUFUNA PEMPHERO LAPADERA KOMASO KUMASULIRA MALOTO KAPENA KULANDIRA YESU KHRISTU KUKHALA MBUYE NDI MPULUMUTSI WA MOYO WANU

TILANKHULENI PA👇

WHATSAP OR CALL
(+265) 992 275 595

HALLELUJAH🙌

07/05/2026

MULUNGU WATHU SALEPHERA

LUKA1:37
YEREMIYA 32:27
YEREMIYA 33:1-3

Nonse amene muli ku South Africa moyo wanu uli m'manja mwa Mulungu

Osadera nkhawa olo pang'ono Mulungu ali nanu mnthawi zonse palipomse.
YESAYA 54 :17

NGATI ULI KU SOUTH AFRICA KAPENA M'BALE WAKO NENA KUTI AMEN

06/05/2026

Chipambano china chimabwera ndi phokoso komanso chisokonezo,Osataya mtima🤷‍♂️,Mulungu sazakusiyani k*t muchite manyazi 🙏. Hallelujah 🙏🙏🔥

06/05/2026

Chipambano china chimabwera ndi phokoso komanso chisokonezo,Osataya mtima🤷‍♂️,Mulungu sazakusiyani k*t muchite manyazi 🙏

Hallelujah 🙏🔥

06/05/2026

Mulungu akukumbukireni nonse amene kwanoko amakudalirani

Chiyembekedzo cha makolo ndi azibale anu chiri pa inu koma zinthu sizikuyenda

Leroli Yehova Mulungu wamphamvu zonse akukumbukireni

Nenani k*ti AMEN

NGATI MUKUFUNA PEMPHERO LAPADERA KOMASO KUMASULIRA MALOTO KAPENA KULANDIRA YESU KHRISTU KUKHALA MBUYE NDI MPULUMUTSI WA MOYO WANU

TILANKHULENI PA 👇

WHATSAP OR CALL

(+265) 992 275 595

Address

Blantyre

Telephone

+265887096964

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when TRUTH MEDIA posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to TRUTH MEDIA:

Share