Ruso xclusive

Ruso xclusive Arts&Entertainment

Mukamakavota musaiwale kuti achina chisale amaba iye ali mtuloKusankha uyu nde bola M C P yomweyi. Wakula uyu
12/09/2025

Mukamakavota musaiwale kuti achina chisale amaba iye ali mtulo
Kusankha uyu nde bola M C P yomweyi. Wakula uyu

02/07/2025

lero ndikumudalisa uyu pangongole😂

Uyu nd nanyoni mzimayi waluso pazisuzoMulungu ndiwabwino🙏
24/06/2025

Uyu nd nanyoni mzimayi waluso pazisuzo
Mulungu ndiwabwino🙏

Israel - Iran update Israel ndi Iran and media houses asimikiza  kuti underground city ya Iran imene amasungilamo zida z...
14/06/2025

Israel - Iran update

Israel ndi Iran and media houses asimikiza kuti underground city ya Iran imene amasungilamo zida zankhondo yapita mbali ina yaphwasulidwa ndi ma Bomba

Last month Iran inajambula pansi pa Nthaka pamene inamanga Malo akulu opangila ndi kusungilamo Katundu.

We are waiting for updates Iran ikayambanso kubwenza tikuuzani .
Apapa zikukhala ngati tikunena mbali imodzi chifukwa mbali inayo sanayambe kuponya ma Bomba mu Israel round 2 koma yalonjeza kuti iponya Lero lomwe

Israel - Iran update Israel yaphulisa Gas plant yaikulu kwambiri mu Iran imene Amadalila popanga project ya Nuclear . An...
14/06/2025

Israel - Iran update

Israel yaphulisa Gas plant yaikulu kwambiri mu Iran imene Amadalila popanga project ya Nuclear . Anthu ambiri afera p***a koma figure tikupasani after verification.

Ndege zidakali kuuluka mwamba mwa Iran .

Nkhondo yavuta

Ku inbox kwabwera funso ili-Kodi laipa nd banjali kapena dziko lomwe ndikukhalali? Or ntchito ndkugwilayi?Kapena komwe n...
07/06/2025

Ku inbox kwabwera funso ili-
Kodi laipa nd banjali kapena dziko lomwe ndikukhalali? Or ntchito ndkugwilayi?
Kapena komwe ndikudyela ndlamazi?? Chakwera wandibalalisa eeee'

27/05/2025

Amene mukupanga date amuna oshota send your account number.

Tinenepo zoona apa Dzikoli likuyenda bwino , amene musakuyenda bwino ndiinuyo inuyo mwazondoka mukuona mosochera. Ubwino...
26/05/2025

Tinenepo zoona apa Dzikoli likuyenda bwino , amene musakuyenda bwino ndiinuyo inuyo mwazondoka mukuona mosochera. Ubwino mukuufuna inuwo nde uti???
Boma ndiliti?????

Mwati zukhala bwa ?????
19/05/2025

Mwati zukhala bwa ?????

   OZIBA YEKHA ALI MMANJA MWA APOLICEMai wa zaka 40, Febbie Robert, amumanga ku Lilongwe chifukwa chonamizila kuti anthu...
18/05/2025



OZIBA YEKHA ALI MMANJA MWA APOLICE

Mai wa zaka 40, Febbie Robert, amumanga ku Lilongwe chifukwa chonamizila kuti anthu osadziwika amuba.

M'mayiyu amene amachita bizinesi yogulitsa mzimbe, pa 13 May adapita kumalo kumene amachitira malonda ake.

Malingana ndi wachiwiri kwa mneneri wa polisi ya Lingadzi a Maria Kumwenda, a Febbie adawayimbila lamya amuna awo kuti anthu osadziwika bwino awaba.

" Ndipo adawauza amuna awo kuti anthu amene awabawa akufuna ndalama zokwanira K500,000 kuti awamasule pamodzi ndi anthu ena 20 amene akuwasunga munyumba imene anthu 14 awapha kale," atero a Kumwenda.

Kutsatira izi amuna awo amayiwa adakanena ku polisi kumene apolisi adapeza kuti a Febbie anali kwa Kamwendo ku Mchinji.

Mayiyu akuyembekezeka kukaonekela kubwalo la milandu posachedwapa komwe akayankhe mlandu opeleka uthenga wabodza.

Pangani follow Ruso xclusive

📌congo
10/03/2024

📌congo

Address

Bangwe
Blantyre

Telephone

+265888960403

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Ruso xclusive posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Ruso xclusive:

Share