Machilitso achilengedwe

Machilitso achilengedwe Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Machilitso achilengedwe, Digital creator, Kanjedza, Lilongwe.
(3)

❤️Timaphunzitsa ma remedy achilengedwe inu kumangowelenga muli kwanu
❤️ Business advertising
❤️ Ndimagulitsa ma herbs osiyanasiyana othandiza matenda ambiri
❤️ pangani follow page yi kuti mupindule nawo

19/09/2025

*👃SIMUKUFUNA MIMBA MUTATHA S*X*

👉 Sungunulani soda mkapu nkumwa pompo-pompo mukangomaliza kusewela.

👉 Sefani phulusa nkuika mkapu, nkuikamo madzi ndi table salt, nkumwa mukangomaliza kusewela.

👉 Imwani aspirin muwiri mmawa kukacha.

👉 Idyani papaya lakupsa kapena/ komanso kutafuna nthanga zake 1 tablespoon, mmawa kukacha.

👉 Tafunani jinja kapena 1-2 teaspoon ya powder wa jinja mkapu ya madzi ofunda.

👉 Imwani kapena bwilani 1 teaspoon ya neem powder.

👉 Black seed ~ Chimodzimodzi ndi neem powder.

19/09/2025

*KUYEZA NGATI MAYI ALI NDI MIMBA*

Tigawaneko zochepa chabe m'mene tingadziwire ngati wankazi ali ndi mimba 🤰🏻🤰🏻kapena ayi🌴 ,

*n**i njira zoyedzera mimba muli ku khomo kwanu.*

Very simple

➖1. *COLGATE* , tengani colgate woyera, ikani mukabotolo koonekera, kozeranimo mikodzo yamamawa, ikhale 5hrs ndipo onani ngati maonekedwe akusintha kusanduka obiriwira ndiye kuti muli ndi mimba 🤰🏻

➖2. *ANYEZI* - tengani ka piece ka anyezi ndikulowetsa mkati kagone konko, mzimayi pomwe ali ndi mimba, kotero kakagona konko, ngati pofika mmawa polankhula kapena popuma akupuma fungo la anyezilo ndiye kuti ali ndi mimba.🤰🏻🤰🏻

➖3. *SUGAR* - ikani ma sapuni awiri kapena atatu a sugar muka botolo, ndipo kodzeranimo, ngati sugaryo akusungunuka ndie kuti mulibe koma ngat pakupanga thovu chabe ndie kuti mwaima.🤰🏻

➖4 - *SOPO* -njira yophweka ina ndikutenga ka pisi ka sopo kukaika mukabotolo, kodzeranimo, ngati mukutuluka ma bubble ndiye kuti mwaima.🤰🏻

➖5- *MIKODZO* - kodzani mikodzo mukabotolo ndipo kakhale pa malo a flat osakakhudza kwa maola 24, dzaoneni ngati pamwamba pakuyandama timadzi toyera ndipo pansi pali mikodzo ndie kuti mwaima 👉🤰🤰🤰

19/09/2025

Nsana
🍀🍀🍀*NGATI MWADWALA NSANA OR CHIUNO* ☘️🍀🍀

KUMASANKHATU NJIRA IMODZI.

▶Izi zimathandiza *nsana ndi mchiuno.*

1🍃: finyilani ma *lemon* mu cup, thilani nchere ndi kumwa

2🍃: Tengani ma piece ten a *garlic* ,muzikazinga mmafuta ophikila mpaka zipange brown,zikazizira muzipaka malo opwetekawo

3🍃: *Ginger* ndi *lemon* ;sendani ginger wilitsani kenako mufinyilemo lemon,zikazizila muzimwa

4🍃: *Phulusa* ;(njila iyi imathandizaso ukagona ndi mkazi waku mwez) Phulusa kuthira mmadzi ndikuthilamo nchere mkumwa

5🍃:muzipanganso ma *exercise*

6.🍃Pedzani Masamba amapeyala okwana 10 ndipo *muwasuke bwino ndi madzi* cholinga muchose ma germs komanso fumbi
🍃Mukatero bwatisani ma cup awiri *mukamaphula pa moto akhale Kuti yapedzeka CUP imodzi*
🍃mudzimwa mulingo umenewu Mmawa uliwonse mukadzuka kupanga izi kwa masiku 15.

17/09/2025

Celebrating my 5th year on Facebook. Thank you for your continuing support. I could never have made it without you. 🙏🤗🎉

17/09/2025

Mwadzuka bwanji team

14/09/2025

Matenda yapakhungu

🤷 Ngati inu muli mmodzi mwa anthu omwe amasautsika ndimatenda yapakhungu ndiwani kuti machilitso alipo ndipo inuyo mukhoza kuchila ndithu,

Ndikudziwa kuti tikati matenda apakhungu ambiri tikuyadziwa monga matenda yomwe amachita attack outermost layer of the skin good example ndi zipere,timatuza tongotuluka pathupi osadziwika mtuwake etc mmene tingathele.

👉Koma apa ndabweretsa chomela chomwe mukuchionacho chomwe inu mungagwiritse ntchito pochiza matenda ngati amenewa apakhungu,

💁 Chofunikila kwambiri pomwe inu mwadwala matendawa 👇

Pezani masamba amtengo umenewu uli pa postyi ,muwasinje mumtondo osathila madzi ayi mpaka zipange chiphalaphala kenako finyakoni madzi yake 👇

👉Muzipaka mmalo onse omwe akhudzidwawo kawiri kapena katatu patsiku until mutawona kuti zatha.

Mukapaka dikilani kwa ma hrs musadasambepo pamalopo kulora kuti thupi liyamwe Mphavu yamankhwalawo.

Mukapanga zimenezi inu mudzachila.

Good Health is my first priority to everyone 🙏

14/09/2025

Kabinde./Kamatila

Awa ndimatenda yomwe sasankha ogwira, amagwila wina aliyese, mwana komaso akulu.

KABINDE iyi ndinthenda yomwe imatchedwaso kuti kamatila, akakhala mwana amakanika upanga chimbudzi, amangolira nthawi ina mwinaso mpaka week kutha.

Wamkukuso naye zimachitika chimodzimodzi.

🤷KOMA NANGA TINGATANI POTHETSA VUTOLI.

👪Tiambe kumbali ya ana

👉 Pezani mizu yakapaza munyike ndikumammwetsa pakasa teaspoon imodzi kawiri patsiku mmawa ndimadzuro until mwanayo atayamba chimbudzicho koma osapitilira five days ayi!.

👉Mwanayo muzimumwetsako timauza pang'ono pomwe mukumusambitsa or kungokoza kuti nthawi ino ndimumwetseko mauza, izi zimathandiza kuti mkaka omwe akuyamwa uzigaika ndipo izi zimachitsaso kuti chimbuzi chisamavute.

👉 Pezani soap wa Neema mudule kapisi kakang'ono ndikukaika kobibilako Mwanayo, izi zimachititsa kuti keep chitila chimbudziko kutelele ndipo izi zimachititsa kuti mwanayo kuchita chimbudzi kukhale kosavuta.

👉👪Mwanayo muzimuyamwitsa pafupipafupi.

🌵🌵🌵🌵🌵🌵🌵🌵🌵🌵🌵🌵🌵🌵🌵🌵🌵🌵

🤷Kwakulu akulu.
👉 Pezani makungwa yampoloni mubwatitse mutaikamo mchere ndikumamwa katatu patsiku madziwo.

👉 Pezani mizu yachitontho mubwatitse ndikumwa madziwo kapu imodzi then mukakhale padzuwa kwa 1hr ikamatha 1hr mukhala mutatsekuka mmimba zikatero 👇 Pezani mizu yamathulisa musinje ndikumwako pang'ono, mudzabwezeretsa chimbudzi.

👉 Pezani mizu yakapaza munyike ndikumamwa madziwo pafupipafupi

14/09/2025

*KODI MUKUDZIWA KUYIPA KOSUNGA MIKOZO❓*

❣️ Ambiri mwa ife tili ndi chisimu chomasunga mikodzo nthupi mwanthu zimene zili zoyipa kwambiri.

-Musamafike pomva kupweteka pachinena chifukwa chosunga mikodzo chifukwa mumakhala kuti mukuononga chinkhodzodzo.
```
-Pamene muchinkhodzodzo mukusungidwa mikodzo zimapangisa kuti mikodzo yomwe ija asanduke miyala yomwe imakhala muchinkhodzodzo chifukwa chosayitulusa munthawi yake.

-komanso mumakhala kuti mukuononga chinkhodzodzo chanu.
```
- Chowopsa choti munthu akafika pamenepa amakhala ndi mavuto ambiri akakhala kuti ndi mamuna kuti agone ndi mkazi wake amapezeka kuti akunthila umuna mwasanga ngakhale atayamba kumene kusiya mkazi asanankhute.

-Akakhala mkazi chilakolako chofuna mamuna chimachoka ndipo umkazi wake umakhala oundana zikafika pamenepa zimamvuta kuchila kwake.

-Pamene mikodzo mukuyikakamiza kuti isatuluke pa nthawi yake,mumakhala kuti mukumasula mabuleki amene amapangisa kuti mkodzo usatuluke wokha komano muchite kutulusa nokha mukafuna.

-Zosatila zake mukakhala kuti mwatelo kumapanikiza nkodzo kuti usatuluke mabuleki amatopa ndipo umafika nthawi yoti umazangotuluka okha popanda kuwulamulila.
```
-`Pamene mwasunga nkodzo zikupangitsa kuti njira ya nkodzoyo ikhumate ndiye zosatila zake ndi matenda acancer ya chinkhodzodzo.

-ukodza kodzo wa chikasu(yellow)dziwani kuti zikapitilila muzadwala matenda akhansa yachinkhodzodzo.

-️ zokudya zozizilitsa kukhosi zimaononga chikhodzodzo chifukwa zimapangitsa chinkhodzodzo kukhala ndi miyala.

-Mukasunga nkodzo nthawi yayitali mapeto ake mumazalila nkodzo wanu womwe mukuvutika kuti mukodze.

-Komanso zikafika potelo nkodzo wake umakhala odula dula mapento ake kaya muli minibusi umazangozindikila kuti nkodzo watuluka wokhala
```
-Tiyeni tipewe kuchita mosusana ndi nthupi lanthu.

-Ngati mwamva chinthu choti mukufuna kupita kukakodza tiyeni mupite nthawi yomweyo ndipo musachedwenso.

-Kondani moyo wanu ndipo tetezani chinkhodzodzo chanu.

10/09/2025

🌾🎋🍃 *KUWAWA KWA MABERE NDI KUWAWA KWA MMA JOINT*

```mabele amawawa munjira zingapo, ena amawawa akamapanga period, ena akangobeleka, komaso Pena olo ukakhara ndi chilakorako amatha kuwawa,pena kusokonekera chake kwama hormones```

*Koma mulungu amatikomera nthawi yose makhwala alipo timatha kuchira muphavu za che bola chikhulupiliro basi*

🥒 _Pezani cabbage leaves,🌱 masamba akabichi ndi makhwala koposa inuyo ingophwaturani kabichiyo masamba awiri ndi kuvalira bra Kwa siku latuthu maberewo amasiya kuwawa,_

```Kapena mupangeni juice, kumuduradula kumugaya kapena kumusinja kuthiramo madzi ndikusefa bwino, kenako ndi kumathila pama bele anuwo sachedwa kusiya kuwawa```

*Ma joints kuwawa*

_Tengani msamba akabichi mangani pa joint pomwe pa kuwawapo Kwa siku lose, kapena muzimata zosinjasinja za kabichi wanu uja kumangapo ndi bandage, olo kasalu kuwawa Kwa ma joint ko kumasiya_

UBWINO OKONDA KUDYA MA ORANGE```Ma orange ndichakudya chabwino kudya chifukwa muli zinthu zambili zomwe ndizofunika kuth...
10/09/2025

UBWINO OKONDA KUDYA MA ORANGE

```Ma orange ndichakudya chabwino kudya chifukwa muli zinthu zambili zomwe ndizofunika kuthanzi lathupi lathu```

```Ngakhale kuti ambili timakonda kudya ma orange koma sitidziwa ubwino omwe umapezeka muma orange```

UBWINO WA ORANGE🍋

```↪ Orange imamupangisa munthu kukhala ndi thupi losalala kotelo kuti chiphuphu sichimaka paiye```

```↪ Orange limapangisa kuti chitetezo chanthupi chikhale chokwanila kotelo matenda amavuta kukhala nthupi, komaso kwa omwe ali postive ndibwino kumadya kwambili ma orange```

```↪ Orange limathaso kuthandizila ntchito yakuchipinda ndipo abambo komaso amayi ngati mukumadya ma orange kwambili muzaona kusintha pakagwilidwe kantchito kuchipinda```

```↪ Orage limamupangisa munthu kukhala mu mood yabwino maka panthawi yomwe waona kuti wabalalika pachina chake inu ingotengani orange mudye muzakhala bwino```

```↪ Mu orange muli vitamin c yemwe amakhala ofunikaso kwambili ku mano anthu choncho kudya ma orange ambili mano anu azakhala olimba```

```↪ Mukamadya ma orange simuzakhala ndi vuto lamaso chifukwa orange limapangisa kuti maso athu aziona bwino ndikuwateteza kumatenda osiyana siyana```

```↪ Ma orange amathandiza kuti ma cells acancer asachuluke mthupi```

```↪ Ma orange amathandizila kugaya chokudya nthupi choncho mukamaliza kudya ndibwino kudya orange kuti digetion izichitika bwino```

```↪Ma orange amathandiza ntima maka pakayendedwe kamagazi komaso amachepesa mafuta nthupi```

```↪ Amathandizaso kuti tsisi lizikhala lokuda bwino komaso silidukaduka```

```↪Ngati muli ndi vuto la asima yambani lelo kukonda kudya maorange muzachila mosavuta```

📍🦜🦜KUPOTOKOLA M'MIMBA🍅🍅🍅🍅🍅🦜🦜🦜🦜🦜🦜🦜🔥Wiritsani ginger wa fresh ndi kumamwa madzi ake...Idyani masamba a Cham'mwamba komanso...
10/09/2025

📍🦜🦜KUPOTOKOLA M'MIMBA🍅🍅🍅🍅🍅
🦜🦜🦜🦜🦜🦜🦜🔥

Wiritsani ginger wa fresh ndi kumamwa madzi ake...Idyani masamba a Cham'mwamba komanso ngati ndiwo....Wiritsani masamba a Gwafa ndi kumamwa madzi ake....Nyikani masamba a Neem osinjasinja m'madzi ozizira ndi kumamwa madzi akewo

*🌀KUWAWA PANSI PA MCHOMBO🌀*

*Pansi pa Nchombo pamawawa maka azimayi ndi ma sister athu akamadwala ku period ngati pali ena omwe mumamva kuwawa even out of pain of period pangani izi*
💠Tengan spoon ya dothi mkuthila mu madzi a half litre
💠Tenganinsoni ndimu limodzi komanso kamchere pang'ono takasani bwino nkumamwa maka mukakhala ku period
*KUVUTIKA NDI PERIOD* 🌷💐

Masamba amango amabwezeretsa system ya period mchimake, ngat period yanu sikuyenda mwa ndondomeko, kusinthasintha ma date opangira period, kutaya magazi kwambiri(heavy period), kusapanga period koma mulibe mimba, kupweteka kwa mmimba popanga period ndi mavuto ena osiyanasoyana okhudza period.

*ZOFUNIKA KUCHITA*

Wilitsani masamba amango nde muzimwa madzi akewo.
KAPENA
Semani makungwa amtengo wamango ndi kuwilitsa ndi kumamwa madzi akewo.

*WARNING!!!*

Masamba kapena makungwa amango si ofunika kumwa kopitilira 3 weeks chifukwa amachepetsa suger mthupi nde suger akachepa dziwani kuti mwapalamula matenda ena

10/09/2025

Mwadzuka bwanji team Machilitso achilengedwe

Address

Kanjedza
Lilongwe

Telephone

+265884009300

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Machilitso achilengedwe posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Machilitso achilengedwe:

Share