
26/04/2024
Nyacksy Pizzo Nyawera anathesa chibwenzi ndi Moreen pa zifukwa zoti..ATI Moreen samatha kuphika, alibe kumbuyo ndi Zina zambiri..
Lero tikumvanso kuti A Nyacksy aja akufuna kuti abwererane ndi Moreen..
Akuti Moreen ndi mwana bullet heavy..
Pangani download nyimbo ya Moreen pa link iyi
https://kkmusic.co.za/play?audio=Maureen
Kenako mumverenso nyimbo yake yomwe akuti X-wanga pa link iyi
https://youtu.be/30f1Vc8oZB0?feature=shared.
Maureen by Nyacksy X Kesi prod by Nyacksy