Malawi Online News Source

Malawi Online News Source For Advertising and Page promotion Call or SMS On: +265986075534
(1)

29/06/2025

Psalm 20:2 (ESV):
“May he send you help from the sanctuary and give you support from Zion!”

Mzuzu International Airport is shaping up nicely👏
28/06/2025

Mzuzu International Airport is shaping up nicely👏

28/06/2025

Dziko langolowa njuga,🙌mawayilesi mma TV nkhani yake ndi njunga basi,,,aaaah zatikwana😭

28/06/2025

Lero ma ukwati nde anabheba mtown mu,🙌Koma tsiku lanu latha bwanji kumeneko???

Mdziko la Iran lero kuli mwambo wa maliro ,akuyika atsogoleri omwe adaphedwa ndi ma missiles omwe Israel imkaponyera Ira...
28/06/2025

Mdziko la Iran lero kuli mwambo wa maliro ,akuyika atsogoleri omwe adaphedwa ndi ma missiles omwe Israel imkaponyera Iran masiku apitawo,,,

28/06/2025

Ambili tikukhulupilira kuti zalowa lero,,,,maluzi kutukwanitsa🙌

Hello Admin I am a Zambian kindly hide my ID. Look Edgar Lungu was treated as a commoner he was not allowed to go outsid...
28/06/2025

Hello Admin I am a Zambian kindly hide my ID. Look Edgar Lungu was treated as a commoner he was not allowed to go outside to access medical facilities and the person who signed for him to go to South Africa at the airport which him lungu built during his time in office was fired.. If the state truly cared about honoring Lungu, why was that dignity not extended when he fell ill? Why was his departure from Zambia treated as that of an ordinary citizen? Lungu left the country stripped of his presidential dignity, denied public respect, and removed from the national consciousness with calculated indifference.

He was not accorded the courtesies of a statesman in life, so why the urgency now in death?

Worse still, the state has not denied reports that the official who facilitated Lungu’s departure at the airport was subsequently fired, a damning signal that his exit was neither welcomed nor dignified. This revelation, first reported by News Diggers, a publication widely seen as echoing state positions, has yet to be challenged by the administration. The silence speaks volumes....

Ndife amodzi,🙏ndale zisatigawanitse🤝
28/06/2025

Ndife amodzi,🙏ndale zisatigawanitse🤝

Arsenal   ikufuna Eberechi Eze yemwe amasewera timu ya Cristal Palace, palace ikumugulitsa katswili yu pamtengo wa 68 mi...
28/06/2025

Arsenal ikufuna Eberechi Eze yemwe amasewera timu ya Cristal Palace, palace ikumugulitsa katswili yu pamtengo wa 68 million Pounds,TottenhamHotspurs nayo yadyerera maso pa osewera yu..

Ku America kuli mtsutso ndi momwe  oimba Ariana Grande akuonekera masiku ano.Akuti wachepa thupi kwambiri, ena akuti woi...
28/06/2025

Ku America kuli mtsutso ndi momwe oimba Ariana Grande akuonekera masiku ano.Akuti wachepa thupi kwambiri, ena akuti woimbayu atha kukhla mmavuto a stress, komanso kusadya mokwanira kutha kupangitsa kuti achepe thupi.koma poyankhula ndi wailesi ina Grande wapempha anthu kuti asiye kupanga za this lake🙌ndipo wati alibe vuto lililonse...

28/06/2025

Masalimo 37 vs 4
"Udzikondweretseso mwa Yehova;
Ndipo Iye adzakupatsa zokhumba mtima wako."

Ana a Mulungu, tiyeni tichite zomukondweretsa Mulungu ndi cholinga chakuti atipatse zokhumba za mitima yathu .👏

Akathidzimula🙄
27/06/2025

Akathidzimula🙄

Address

Chichiri
Blantyre

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Malawi Online News Source posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share