19/02/2026
BUSINESS & ENTREPRENEURSHIP CONFERENCE
Pambali pakuchita bwino ndi business yochepa pamakhala wina waikapo moyo ndi ntima wake kuti zitheke
BUSINESS SEMINAR
tikhala ndi business seminar pa 28 February 2026 ( Saturday ) kwa ochita malonda komanso kwa ofuna kuyamba business mukuitanidwa kudzatenga mbali🙌
MAGAWO A SEMINAR
👉business system
👉 Passive and active business
👉Building generation wealth
👉How to raise enough money to start your personal business without loan
MALO
✏️Blantyre, mpemba kalitsilo cbo_
STANDARD FEE
Before day
👉K2,000
Kudzalipira pakhomo k4000
EXCUTIVE FEE
Kulipiliratu 👉K5000
Kudzalipila pakhomo k10, 000
TIME TO START
👉 12pm until 4:30pm
NOTE
We ask you to dress smart or decent on this day👔👖
PAYMENT ACCOUNTS
AIRTEL MONEY
📱0998889119
MPAMBA
📱0883330805
FOR MORE
0998889119
GULIRANITU TIKET YANU NDIYA OKONDEDWA ANU TSIKU LISANAKWANE