Che Senza

Che Senza Music is Life,��

04/05/2025

“If milk gets bad, it becomes yoghurt. Yoghurt is more valuable than milk. If it gets even worse, it turns to cheese. Cheese is more valuable than both yoghurt and milk.

And if grape juice turns sour, it transforms into wine, which is even more expensive than grape juice. You are not bad because you made mistakes. Mistakes are the experiences that make you more valuable as a person.

Christopher Columbus made a navigational error that made him discover America. Alexander Fleming’s mistake led him to invent Penicillin. Don’t let your mistakes get you down.

It is not practice that makes perfect. It is mistakes we learn from that makes perfect.”

Credit goes to respective owner

02/05/2025

Munthu wabwino iwe, ukaona moyo umauona motani??

Anthu amati Moyo umayenda mu ma phase osiyana siyana.Izi ndi zoona koma ndikuuzani Maganizo anga kapena kuti opinion yanga.
Chomwe ndaona mu zaka 25 zomwe mulungu wandisunga nazo pa dziko pano. Moyo umayenda mu ma phase/step ndithu ndiponso mu moyo kuphunzila sikumatha.

kuphunzila kumayambila tsiku Lomwe mulungu wakuika pa dzikoli. chilichonse timachita kuphunzila ndithu kuchokela tsiku lobadwa mpaka tsiku lomwalila.

Nde pali kuphunzila muzolakwika zathu. ngati sunalakwitse ndekuti sungaphumzile, sinanga walondola kale nde uphumzila chaninso pamenepo? koma ukalakwitsa mpomwe umadziwa pomwe zinthu sunaziyendetse bho nde umaphunzila. ngati wabweleza kulakwitsa kwako ndekuti sunaphunzilebe ndipo uzipitilila kulakwitsa mpaka utamphunzila.

moyotu ndi ophweka koma anthu timauvutitsa tokha. we are here to learn from what life give us in every day situations, ndipo tikhala tikuphumzilabe mostly muzolakwitsa zathu so let's embrace our imperfections.

ndatha ine wanu,

CheSenza

failures

03/01/2025

Am back with a different vide, stay tuned good people.😎

Okuba mantha awachokela ndithu, eti mpaka kuba mukachisi🤣🤣
21/10/2024

Okuba mantha awachokela ndithu, eti mpaka kuba mukachisi🤣🤣

She Didn't Know She Was Seating Next To A Future "Global Star" ☺️ osazaiphweketsa nthawi.
21/10/2024

She Didn't Know She Was Seating Next To A Future "Global Star" ☺️ osazaiphweketsa nthawi.


19/10/2024

Ati akanandilola koma ku Facebook profile kwanga kulibe ma pic a Graduation.,😆😆

Kopita Friday kuja kwapezeka🔥🔥🔥achina FADA Motionist achita bwino akubwera ku Mangochi.
16/10/2024

Kopita Friday kuja kwapezeka🔥🔥🔥achina FADA Motionist achita bwino akubwera ku Mangochi.

12/10/2024

Aaah boys akazi ambili a a nyash nde ndi mbutuma zenizeni.. osaitengela nyash.😂😂😂

Some of the reasons why women live a long life than men🤣🤣🤣
11/10/2024

Some of the reasons why women live a long life than men🤣🤣🤣

11/10/2024

I agree 💯💯💯

Ndinkangomva zoti mzuzu is a green city.. eeeh it's indeed green and beautiful.. Mzuzu City👇👇😆
09/10/2024

Ndinkangomva zoti mzuzu is a green city.. eeeh it's indeed green and beautiful.. Mzuzu City👇👇😆

Good morning people...  Chimfine si zinthu eeeeh🤧
09/10/2024

Good morning people... Chimfine si zinthu eeeeh🤧

Address

Blantyre
SOCHE

Telephone

+265882398832

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Che Senza posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Che Senza:

Share