30/09/2026
Please hide my ID. Since some guys are sharing stories here., post me too. Of course ineyo sikuti nakumana ndi mkazi pa app yanu, no. Koma inali cross ya MR p k*k i paid connection fee ndithu 50k. So here’s the thing. Mkazi yu amakonda kupanga post ma meme tonyoza broke ni**as k*k. Makamaka pa tik tok amakonda tima video tija amakhala ngati akuyankhula koma voice ya munthu wina.
Ngati apapa waika akuti look for a man who can take you out, buy you an expensive wig if he is broke dump him k*k nde ine ndikafumsa amati babe its just content. Koma sitinganene kuti munthuyi ndekuti content iyi akugwirizana nayo? As in its her charecter. Nanga munthu atapanga video ya satanic yonyoza yesu angapange share sound yake her being a Christian.? Komaso cant we say kuti iyeyu apapa akuitanira malonda kuti amuna andalama amulowe inbox and give her offers? Komanso munthune am broke ndithu. Nde zumandidabwisa. Pali love pamenepa kapena nditenge tanga tochepa ndisake nzanga otchipa?