NewsRoom Malawi

NewsRoom Malawi Factual news from Malawi and across the World

25/02/2026
Kugulitsa wosewera modzi yetha, FCB Nyasa Big Bullets yapeza ndalama zoposo zikho zonse za m'Malawi muno.
20/01/2026

Kugulitsa wosewera modzi yetha, FCB Nyasa Big Bullets yapeza ndalama zoposo zikho zonse za m'Malawi muno.

20/01/2026

In less than 4 months time fuel has gone up by 96%.
😭😭😭😭😭

BREAKING!Mtengo wa mafuta a galimoto wakwera ndi 41% kuyambira  lero pa 20 January 2026.Petrol wafika pa K4,965 kuchoker...
20/01/2026

BREAKING!
Mtengo wa mafuta a galimoto wakwera ndi 41% kuyambira lero pa 20 January 2026.
Petrol wafika pa K4,965 kuchokera pa K3,499.
Diesel wafika pa K4,945 kuchoka pa K3,500.

Bugwe la MERA lasindika za kukwera mtengo wa mafutaku kuzera muchikalata chimene akututsa m'mbanda kucha wa lero.

Moses Kunkhuyu wayitanidwa ku Area 30 police kuti akayankhe mafunso.We will keep updated.
19/01/2026

Moses Kunkhuyu wayitanidwa ku Area 30 police kuti akayankhe mafunso.

We will keep updated.

A strong second-half response saw FCB Nyasa Big Bullets overturn an early deficit to secure a 3–1 victory over Ndirande ...
18/01/2026

A strong second-half response saw FCB Nyasa Big Bullets overturn an early deficit to secure a 3–1 victory over Ndirande Stars.

FAM President Fleetwood Hayiya walamula a Walter Nyamilqndu kuti awalipire K200 million pasanathe matsiku anayi chifukwa...
18/01/2026

FAM President Fleetwood Hayiya walamula a Walter Nyamilqndu kuti awalipire K200 million pasanathe matsiku anayi chifukwa za zimene adawuza tsamba la mchezo la face 2 face kuti a Hayiya anagwilitsa ntchito zipolowe mu 2023 kuti apambane pa mpando wa mtsogoleri wa FAM.

BREAKING NEWS: Yoweri Kaguta Museveni Tibuhabura is officially re-elected as President of the Republic of Uganda for the...
18/01/2026

BREAKING NEWS: Yoweri Kaguta Museveni Tibuhabura is officially re-elected as President of the Republic of Uganda for the 2026–2031 term.

As it stands Yoweli Museveni is the President elect, while we are waiting for official announcement by Uganda Electoral ...
17/01/2026

As it stands Yoweli Museveni is the President elect, while we are waiting for official announcement by Uganda Electoral Commission.

Address

Victoria Avenue
Blantyre

Telephone

+265888699130

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when NewsRoom Malawi posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to NewsRoom Malawi:

Share