
09/08/2025
Minibus yagwera kuphompho pa Bale mu msewu wa M1 ku Rumphi.Driver wa basiyo amaopa kuombana ndi truck pa gulaye ina ya pa malopo ndipo adaganiza zongoilowetsa kutchire.Akuti palibe wavulala modetsa nkhawa pa ngoziyo.
Thank God onse alimoyo ๐๐พ