Mpatsa onyekwe

Mpatsa onyekwe Entertaining and spread news all over the world 🔥

Trending model 🔥🔥🔥🔥Small wifey🙌
08/07/2025

Trending model 🔥🔥🔥🔥

Small wifey🙌

Bullets is expected to deal with civil service this coming Saturday at get ready....mauleeeeeeee🔥🔥🔥🔥🔥
08/07/2025

Bullets is expected to deal with civil service this coming Saturday at get ready....mauleeeeeeee🔥🔥🔥🔥🔥

With international duty behind us and fresh energy in the camp, The People’s Team is back to work and fully locked in on the next mission: an away test against Civil in the capital this Saturday.

Waakulu a ginte🙌
08/07/2025

Waakulu a ginte🙌

Lelo mamawa president Donald Trump alamula kuti USA ipitise Zida zankhondo zoophya Ku Ukraine kuti aziteteze Ku Russia.I...
08/07/2025

Lelo mamawa president Donald Trump alamula kuti USA ipitise Zida zankhondo zoophya Ku Ukraine kuti aziteteze Ku Russia.

Izi zachitika pamene President Trump anaimbilana phone ndi President Putin kuti nkhondo ithe koma President Putin anakana Anati until alande Ukraine yonse .

Kenako President Trump anaimbilanso President wa Ukraine amene Anati ndi okonzeka kuti ithe

Good morning family 🔥🔥
05/07/2025

Good morning family 🔥🔥

22/06/2025

Iran - Israel updates

EU yayankha kuti mesa poyamba mwakhala mukukana kuti simukupanga ma nuclear Lero mamawa mwavomeleza ndi kulumbila kuti simungasiye. Ndiye mumanamilanji?

Simungabisale pamaso pa USA

Mumafuna muzipusisa anthu ndizokambila kuti muzikana pansi pansi mukukonza ?

Nanga Ku Geneva Ko Mesa munakanisisabe kuti simusiya .

Tikukuitananinso Ku meeting yomaliza kuti musaine kuti kutsogolo kuno simuzapanganso za nuclear .

Iran - Israel updates Foreign minister wa Iran Wauza European Union kuti Tsiku limene  Iran ndi USA ndi Israel anakonza ...
22/06/2025

Iran - Israel updates

Foreign minister wa Iran Wauza European Union kuti Tsiku limene Iran ndi USA ndi Israel anakonza Zokambilana zokhuza kuti asiye kupanga za nuclear pa 12 June mwezi omweo uno mamawa lake Israel inabwera kuzawapanga attack .

Dzana meeting inaliko ku Geneva timakambilana Lero mamawa USA yatiphulisa

Ndiye mukamati Mufuna kukambilana ndi Iran mukutanthauza chani maka maka.

Will update EU ikayankha

Iran - Israel updates Pakistan yatseka Border yake kuti anthu ochoka Ku Iran pothawa nkhondo asalowe mudziko Mwake .Iyo ...
21/06/2025

Iran - Israel updates

Pakistan yatseka Border yake kuti anthu ochoka Ku Iran pothawa nkhondo asalowe mudziko Mwake .

Iyo yati sikufuna kukhuzidwa ndi nkhondo imenei

21/06/2025

Israel - Iran update

Israel yachotsa Moyo wa Commander wa Iran Wachiwiri UAV unit ya IRGC Dzina lake Amin Pourjodki mamawa Uno

Pa list ya target pasala anthu 9 imene Israel inaika

19/06/2025

Israel - Iran war

Mawa Iran , European Union ndi UK akonza meeting kuti akambilane Mene Nkhondo ingathere .
Iran yapanga confirm kuti Ipanga attend .

Amene akaimile Iran ndi Abbas Araghchi. Foreign minister

Will update

Israel - Iran update Israel yaphulisa Internal security head Quarters ya Iran  10 minutes ago .Air force jets ndi zimene...
18/06/2025

Israel - Iran update
Israel yaphulisa Internal security head Quarters ya Iran 10 minutes ago .

Air force jets ndi zimene zikusakaza. Iyi inali central Command ya Supreme Leader

Mu chithunzi ndi Ndege za airfoce being used .

Take note that Iran sikuponya Kaye mabomba mu Israel

Address

Blantyre

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Mpatsa onyekwe posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share