Director Khober

Director Khober Video Grapher/Photographer

Oky za bho bho ๐Ÿ˜‚
09/09/2026

Oky za bho bho ๐Ÿ˜‚

Mwati ndikuti uku nanga chikuchitika ndi Chan tipaseni map tikajoine nawo ๐Ÿ˜‚๐Ÿคซ
09/09/2026

Mwati ndikuti uku nanga chikuchitika ndi Chan tipaseni map tikajoine nawo ๐Ÿ˜‚๐Ÿคซ

APA SIZINAYENDE ๐Ÿ™‰๐Ÿšซ๐Ÿ“ต
08/09/2026

APA SIZINAYENDE ๐Ÿ™‰๐Ÿšซ๐Ÿ“ต

07/09/2026

๐Ÿ™„

A POLICE amanga iPhone Daddy๐Ÿ”— chifukwa chobela munthu wina ndalama๐Ÿ’ต๐Ÿ’ถ yemwe amafuna kugula iphone ndipo anamuuza kuti  at...
07/09/2026

A POLICE amanga iPhone Daddy๐Ÿ”— chifukwa chobela munthu wina ndalama๐Ÿ’ต๐Ÿ’ถ yemwe amafuna kugula iphone ndipo anamuuza kuti atumiza half ya ndalama kt inayo azamalize akamazatenga phone koma zapezeka kt atangotumiza ndalama phoneโŽ๐Ÿ“ณ samayankha ndipo sanayeleke kt apite akamalize business yawo ndipo patatha sabata munthuyu anakapeleka report ku police moti tikunena pano mnyamata otchedwa iPhone Daddy Ali NCHITOKOSI ๐Ÿ”—

๐Ÿšซ๐Ÿ“ต

Apa nde idyedwa yosasosolatu ๐Ÿ˜‚๐Ÿ™‰
07/09/2026

Apa nde idyedwa yosasosolatu ๐Ÿ˜‚๐Ÿ™‰

Azibambo amatsiku anofe ndife azimayi pomwe azimayiwa ndazibamba mwamvesesa kapena ndifotokoze bwino bwino ๐Ÿ˜‚๐Ÿ™‰
07/09/2026

Azibambo amatsiku anofe ndife azimayi pomwe azimayiwa ndazibamba mwamvesesa kapena ndifotokoze bwino bwino ๐Ÿ˜‚๐Ÿ™‰

Mwati zukhala bwanji apa wina atifotokozeleko๐Ÿ˜‚๐Ÿ™‰
07/09/2026

Mwati zukhala bwanji apa wina atifotokozeleko๐Ÿ˜‚๐Ÿ™‰

Nde kuli iyi yomaphika nyemba utayikamo khala kaya zimatanthauza chani tichoseni umbuli๐Ÿ˜„๐Ÿคฃ๐Ÿ™‰
06/09/2026

Nde kuli iyi yomaphika nyemba utayikamo khala

kaya zimatanthauza chani tichoseni umbuli๐Ÿ˜„๐Ÿคฃ๐Ÿ™‰

izi kwanuko mmazitcha chani??
05/09/2026

izi kwanuko mmazitcha chani??

Address

Phoenix
Blantyre

Telephone

+265885835468

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Director Khober posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share