Ice the Journalist

Ice the Journalist Entertainment and breaking news and some follow ups

Holiday Season 1 EP 1
10/08/2025

Holiday Season 1 EP 1

With Kante Visuals – I just got recognized as one of their top fans! 🎉
10/08/2025

With Kante Visuals – I just got recognized as one of their top fans!
🎉

23/07/2025

Dir Holice akuti akupita chitsogolo,Chisana kapena Chisiku Zikomo🇲🇼

23/07/2025

Ma Designer ali komkuno ku Malawi zikomo🕴

07/07/2025

dzina langa ndine Sikono
Zikomo mu tikufelanji ndizawoneka kumapeto(Ndatero)

07/07/2025

Gold Mining Akuti yavuta Ku Balaka Livilizi
akutero Tamandani Chidothi from MIj khangati

I was about kupanga nyama nseula today morning ndangosiya grinded nseulaBoss ndinu dolo
07/07/2025

I was about kupanga nyama nseula today morning ndangosiya grinded nseula
Boss ndinu dolo

Israel - Iran updates

Kuyamba last week Gulu la Iran lotchedwa Houthi Ku Yemen lakhala likuphulisa Madela Aku Israel . 3 days ago anatumiza mabomba kuphulisa mbali ya airport ya Israel tinanena.
Israel inapeleka warning . Dzulo gulu Ili linayamba kuombela Sitima ya Israel yodusa mu red sea.

Mamawa Uno Israel yanyamuka ndipo yayamba kuphulisa ma port onse a Dziko la Yemen . Israel yalengeza kuti wina aliyense asamuke Ku chigawo ichi chifukwa within 48 hours dela Ili lonse litentha Moto.

Chithunzi ndi chalero Israel yayamba kutentha moto Dziko la Yemen chigawo chaku ma port

07/07/2025

I wish ndikanakumana ndi Duma Ku Lilongwe komko after late magufuli we link 2010
Happy Birthday Makhilikhili

07/07/2025

ICE THE JOURNALIST YAFIKA PA NIGERIA(SPACE ONLINE)On the move.

Address

Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Ice the Journalist posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share