Biggie Lu

Biggie Lu Musician, Entrepreneur, Event Planner & Host. is a Malawian recording artist, Born and raised in Malawi, Blantyre.
(1)

Tel Aviv Yafo!
20/09/2025

Tel Aviv Yafo!

18/09/2025

Koma anthu tili ndi ma Surname eh 🀣

Ndaona mkazi wina wake Surname yake ati NDEVUZAMWAYI ah πŸ˜…πŸ˜…

Kwao anthu ndekuti akangotuluka ndevu zimakhala za Mwayi

18/09/2025

Mu Chi Nkhonde timati "Kufyula" mu Chitumbuka amati "Kukhwengwena" ndipo mu chichewa amati "Kuse... 🀣🀣

Basi ife ana ADAD

Mmene zikuonekera apamu, DPP nkupezeka yaluza eh koma kungakhale nkhondoπŸ˜…πŸ˜…πŸ€£
18/09/2025

Mmene zikuonekera apamu, DPP nkupezeka yaluza eh koma kungakhale nkhondoπŸ˜…πŸ˜…πŸ€£

Muchipululu simofera πŸ˜…
18/09/2025

Muchipululu simofera πŸ˜…

17/09/2025
Ndapezeratu change amwene Cha after election's!Secure the bag gents πŸ₯±
17/09/2025

Ndapezeratu change amwene Cha after election's!

Secure the bag gents πŸ₯±

Ka bufen ndi ka Mankhwala ka BP kakhale pafupi
17/09/2025

Ka bufen ndi ka Mankhwala ka BP kakhale pafupi

16/09/2025

Tiyeni tikavote β˜‘οΈπŸ—³οΈ

15/09/2025

Ine ndivotera.........

15/09/2025

Azungu akuno πŸ˜…

Busy kumvera English music koma ayankhulise ngendeyo uwone kukuzemba kwake. πŸ˜…πŸ˜…πŸ€£

Umva No Inglisi

Another Monday to Win!Wishing you all tsiku lopambana ndi chimdalitso πŸ«‘πŸ™
15/09/2025

Another Monday to Win!

Wishing you all tsiku lopambana ndi chimdalitso πŸ«‘πŸ™

Address

Myuziki Pusha Entertainment
Blantyre
265

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Biggie Lu posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Biggie Lu:

Share

Musician and Entrepreneure

We are professional at delivering art in package