Sapitwa News Agency

Sapitwa News Agency Freedom of Expression; Our Birth Right!

Chipani cha MCP chati chipani cha DPP ngati chikufuna kutenga Boma chibwele pa "ground".Malingana ndi Jessie Kabwila m'n...
03/07/2025

Chipani cha MCP chati chipani cha DPP ngati chikufuna kutenga Boma chibwele pa "ground".

Malingana ndi Jessie Kabwila m'neneri wa MCP, chipani cha DPP chikuona kuti "game yadula kumaoda mpake akuyambitsa ziwawa mdziko muno"

Kabwila waonjezeranso kunena kuti chipani cha DPP chikafuna kupanga zionetsero chizibwela ndi mtsogoleri wawo Peter Mutharika yemwe iye wati "wakula".


By UKATIULODZWE PHIRI

  Bungwe la Copyright Society of Malawi (COSOMA) ligawa ndalama zoposa 1.5 billion Kwacha kwa anthu a ntchito za luso ku...
03/07/2025


Bungwe la Copyright Society of Malawi (COSOMA) ligawa ndalama zoposa 1.5 billion Kwacha kwa anthu a ntchito za luso kudzera mu ndalama zomwe limatolera kwa anthu ogwilitsa ntchito lusoli, ndondomeko ija yomwe imatchedwa; Blank Media Royalty.

Ndalamazi ndi zokwera kuyelekeza ndi zomwe linagawa mu mwezi wa October chaka chatha zomwe zinali 917 million Kwacha.

Malingana ndi kalata yomwe bungweli latulutsa 1 billion Kwacha ipita kwa aluso a ntchito yoyimba 2999, pomwe 522 million Kwacha ipita kwa aluso lolemba mabuku 565. Ndalamayi ndi yokhudza uthenga omwe bungweli linatolera kuchoka mwezi wa April chaka chatha kufika March chaka chino.

Ndalamazi adzazigawa lachiwiri pa 8 July, sabata yamawa ku ofesi zawo.
(by UKATIULODZWE PHIRI)

NEWSPresident Lazarus Chakwera has come under fire from critics who have described as mere rhetoric his directive for an...
29/06/2025

NEWS

President Lazarus Chakwera has come under fire from critics who have described as mere rhetoric his directive for an investigation into the violence that marred peaceful protests in Lilongwe on Thursday.

During the protests, unknown panga-wielding thugs severely assaulted activist Sylvester Namiwa together with other protesters in full view of police—an act that has received widespread condemnation, with the European Union threatening to withdraw aid.

  The European Union (EU) has threatened to withdraw support for police training in Malawi following violent attacks on ...
27/06/2025


The European Union (EU) has threatened to withdraw support for police training in Malawi following violent attacks on protestors in Lilongwe yesterday.

EU Ambassador to Malawi, Rune Skinnebach, condemned the incident, which occurred in full view of Malawi Police Service (MPS) and Malawi Defence Force (MDF) personnel who did not intervene.

“I was shocked, disappointed and disgusted by yesterday's events,” he told Sapitwa News Agency .

“We have been giving support to police training but that is something we will have to reconsider if the police does not make good use of the training, if they seemingly don't intend to play their role and if their mandate is undermined by instructions from somewhere else,” he said.

Skinnebach added that the EU expects a thorough investigation to identify and hold accountable those behind the attacks.

By UKATIULODZWE PHIRI

 : Gulu la zikwanje laotcha galimoto yomwe inanyamula zida zoyimbira komanso minibus yomwe inaikidwa pa bwalo la Lilongw...
26/06/2025

: Gulu la zikwanje laotcha galimoto yomwe inanyamula zida zoyimbira komanso minibus yomwe inaikidwa pa bwalo la Lilongwe Community.

Izi zachitika apolisi komanso asilikali a MDF alipamalo pomwepa.

Maxwell Mwachande yemwe ndi mwini wake wa minibus yomwe yawotchedwa wawuza kuti wamenyedwa kwambiri galimoto yake asanaiwotche.

Pakadali pano a Sylvester Namiwa sakuziwika komwe ali ndipo anthu omwe anyamula zikwanje komanso apolisi akuzungulira town ya Lilongwe.

Timu ya FCB Nyasa Big Bullets lero ikhala ikusewera mpira ndi timu ya Moyale mu TNM Super League.Ku Lilongwe Silver Stri...
25/06/2025

Timu ya FCB Nyasa Big Bullets lero ikhala ikusewera mpira ndi timu ya Moyale mu TNM Super League.

Ku Lilongwe Silver Strikers FC ikhala ikusewera ndi Karonga United. Ndipo Civo Service iswana ndi Creck Spotting. Chitipa FC vs Songwe FC.

Chipani cha DPP chamemeza a Malawi kuti apite nawo ku zionetsero zomwe bungwe la Citizens for Credible Elections lakonza...
25/06/2025

Chipani cha DPP chamemeza a Malawi kuti apite nawo ku zionetsero zomwe bungwe la Citizens for Credible Elections lakonza mawa pa 26 June mu m'zinda wa Lilongwe.

Zionetserozi ndizokakamiza wapampando wa bungwe la MEC kuti atule pansi udindo.

  A grouping called "Citizens for Credible Elections" has notified the Lilongwe district council of its intention to hol...
20/06/2025



A grouping called "Citizens for Credible Elections" has notified the Lilongwe district council of its intention to hold peaceful demonstrations aimed at forcing the resignation of MEC chairperson Justice Anabel Mtalimanja and the MEC's chief elections officer Andrew Mpesi.

The group's coordinator, Sylvester Namiwa, says the protests will take place on Thursday, 26th June 2025. Namiwa believes the duo are too compromised to preside over free, fair and credible elections.

"The duo's partisan conduct, clearly manifested by the MEC's rejection of demands by electoral stakeholders to allow an independent audit of the Election Management System while clinging to the use of Smartmatic-supplied devices, is enough evidence for their removal," said Namiwa.

While confirming receipt of the letter, Lilongwe district council spokesperson Andrew Mkonda has, however, highlighted that the receipt of the letter does not give the grouping a guarantee to go ahead because the district commissioner will soon call for a stakeholders meeting on the same.

The Malawi Electoral Commission has been addressing such concerns through media briefings and special programmes aired on Zodiak and other media outlets.

   Mtsogoleri wadziko la Iran wawopseza mtsogoleri wadziko la America Donald Trump kuti awona zoopsa ngati asilikali adz...
18/06/2025



Mtsogoleri wadziko la Iran wawopseza mtsogoleri wadziko la America Donald Trump kuti awona zoopsa ngati asilikali adziko lawo alowelele nkhodo yawo ndi Israel.

Iye amayankhula pakanema yaboma mdziko la Iran.

Ayatollah Ali Khamenei wati iwo sagonja pankhondo yomwe ali nayo ngati momwe amafunira Donald Trump.

Pakadali pano Trump wauza mtsogoleri wadziko la Iran kuti agonje pankhondo yomwe ilipo.

   M'tsogoleri wa chipani cha UTM  Dr Dalitso Kabambe, wapereka ndalama ku MEC kuti azapikisane nawo pa Chitsankho chomw...
17/06/2025




M'tsogoleri wa chipani cha UTM Dr Dalitso Kabambe, wapereka ndalama ku MEC kuti azapikisane nawo pa Chitsankho chomwe chichitike mwezi wa September m'dziko muno

    Israel and Iran began a fresh round of attacks on each other Monday, with the death toll mounting and the chance of ...
16/06/2025




Israel and Iran began a fresh round of attacks on each other Monday, with the death toll mounting and the chance of a quick victory for Israel evaporating as the conflict entered its fourth day.

Responding to new Israeli strikes on in Iran, Iran’s Islamic Revolutionary Guard said it had launched its own wave of missile attacks on Israel “with greater force and intensity than before.”

Israel, which launched the latest conflict Friday, said it had achieved “full aerial superiority” over Iran’s capital, Tehran, likening the conditions to its dominance over the Gaza Strip and Lebanon.

At least 224 people in Iran have been killed since Israel’s initial attack Friday, Iranian state media reported, while 24 people have been killed by Iran’s retaliatory strikes against Israel.

Read more: https://nbcnews.to/4e3T9QV

Address

Blantyre

Telephone

+265995004025

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Sapitwa News Agency posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share