EngAllan

EngAllan Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from EngAllan, Digital creator, kanjedza Blantyre, Blantyre.

Kunoso kwacha bwino ndithu!
06/01/2026

Kunoso kwacha bwino ndithu!

Mabulosi😀
05/01/2026

Mabulosi😀

America inapha Sadam Hussein pa 30 December 2006 ndipo  anachita kumukhweza anthunso ambiri anawona. Pa 11 October 2011 ...
04/01/2026

America inapha Sadam Hussein pa 30 December 2006 ndipo anachita kumukhweza anthunso ambiri anawona. Pa 11 October 2011 anapha Muama Gadaffi wathuwathu ku Africa komkuno maiko onsewa akuwona kungompekera zifukwa zopanda pake pomati ndi dictator ngakhale k*ti anthu ku Libya 🇱🇾amkasangala kusiyana ndimomwe zili pano ndipo Mugabe yekha ndiye anadzudzura Nato. Lero agwira Nicholas Maduro ndipo ndili pano mumva k*ti wagamulidwa zoti aphedwe apo ayi kukamusunga kundende yoipa cholinga akafere komko ndi matenda poti wakalowa kale mu court ku New York. Akafuna kupha mtsogoleri amagwiritsa ntchito anthu amu dzikolo zizikhala ngati k*ti anthu mukuvutika ndi utsogoleri ulipowo kenako abwere mu dzina loti tikudzathandiza anthu, umu ndimomwe America yakhala ikuchitira. Gadaffi anamupha chifukwa amkawuza atsogoleri ena mu Africa muno k*ti ndibwino tipange umodzi nakhala ndi President m'modzi oimira Africa, Army imodzi, Polisi imodzi, Ndalama imodzi, Chilankhuro chimodzi. Apa America inadziwa k*ti Africa ingakhale yamphamvu choncho zimenezo zisapitilire ndiye anaganiza zopha amene amkayambitsa zoterezi. Ikondeni America 🇺🇸 chifukwa chaumbuli wanuyo koma kunena zoona samatifuna olo pang'ono. Mwachitsanzo pa South Africa p***a apa pakamachitika Xenophobia kumaphana tokhatokha America siyimakwiya nazo koma muwone Parliament yaku South Africa itangovomereza k*ti azungu alandidwe malo munawona koma zomwe America 🇺🇸 inachita ku dziko la South🙌 poikhaulitsa? Lero akufuna kupha Maduro ndipo kumbukirani k*ti komwe kwatsala tchire ndikomwe moto umalowera. Ku Iran 🇮🇷 ayambitsa mademo cholinga anthu tiziti boma lakumeneko ndi lankhanza apezerepo mwayi wopha amene akumufuna, umu ndimomwe America 🇺🇸 imachitira. Umbuli ndi matenda, ine kwanga ndikunena ngamo.

Ndatha ine wanu

EngAllan

Final of Loser’s Bracket 🔥LIU CHENG-CHIEH 🇨🇳VS WU ZHEN YU🇨🇳
03/01/2026

Final of Loser’s Bracket 🔥
LIU CHENG-CHIEH 🇨🇳VS WU ZHEN YU🇨🇳

Paja ankanena k*t ng'ona ilibe mabere Koma lero yapezeka ili ndi mabere ndipo ndiwoyimaso njiiiii sanagwe
03/01/2026

Paja ankanena k*t ng'ona ilibe mabere Koma lero yapezeka ili ndi mabere ndipo ndiwoyimaso njiiiii sanagwe

Happy New Year! 🎉As we step into this new year, I’m grateful for all the lessons, growth and blessings that came with la...
01/01/2026

Happy New Year! 🎉
As we step into this new year, I’m grateful for all the lessons, growth and blessings that came with last year. 2025 was a good year and I thank God for it.
I pray that this new year will be even better, full of good health, success, peace and amazing opportunities for us all. May our efforts be rewarded and our dreams take shape.
Cheers to a new year and new possibilities! 🙏✨

Mauthenga achisoni akupitilira kuperekedwa k*tsatira imfa ya aluso asanu omwe afa pa ngozi ya galimoto dzulo.Oyimba koma...
27/12/2025

Mauthenga achisoni akupitilira kuperekedwa k*tsatira imfa ya aluso asanu omwe afa pa ngozi ya galimoto dzulo.

Oyimba komanso anthu osiyanasiyana alemba mauthenga awo achisoni pamatsamba awo amchezo kusonyezo kukhudzika kwawo ndi imfayi.

Ena mwa aluso komanso oimba omwe apereka mauthenga awo ndi monga Lulu, Gwamba, Driemo, Steve Muliya, Tuno komanso Robert Chiwamba.

Pakadali pano chipani cha UTM kudzera mu kalata yomwe chatulusa chati ndichokhudzika ndi imfayi.

Icho chati alusowa amatenga nawo gawo polimbikitsa chikhalidwe komanso posangalatsa anthu m'dziko muno.


-Joseph Mphiya-

24/12/2025

Mmmm komaso bodza Ili, koma awawa amadziwa k*ti 30 tonnes ndi truck yaikulu? Ndiye 30 Million ungatengere mu truck?

Visited St Peters Anglican cathedral, built in the early 1900s by the Universities’ Mission to Central Africa (UMCA) and...
21/12/2025

Visited St Peters Anglican cathedral, built in the early 1900s by the Universities’ Mission to Central Africa (UMCA) and it’s one of the most famous landmarks on Likoma Island and on Lake Malawi.

21/12/2025
20/12/2025
Zlatan Ibrahimović: “The last time I cried, was when I didn't receive my paycheck and wages from Malmo FF. I wrote to th...
18/12/2025

Zlatan Ibrahimović: “The last time I cried, was when I didn't receive my paycheck and wages from Malmo FF. I wrote to the league board and asked them to deduct every three points I won for Malmo FF.

The board said: “My money was being paid to my parents because I was too young by law to receive an official salary.”

I told the league board that I was also too young to be the top scorer and win Malmo a league title by law, so they must not be given my 3 points till I am old enough. The next day my money was transferred to my account. I am older than the law.”

[]

Address

Kanjedza Blantyre
Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when EngAllan posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share