Spotlight Waves

Spotlight Waves Home of entertainment

Happy birthday Joe Kellz , mkulu amaimba uyu
13/09/2025

Happy birthday Joe Kellz , mkulu amaimba uyu

Happy birthday Giboh Pearson 🎂
29/08/2025

Happy birthday Giboh Pearson 🎂

A Princess chitsulo vumbulukani komwe muliko anthu asowa nyimbo zanu
23/08/2025

A Princess chitsulo vumbulukani komwe muliko anthu asowa nyimbo zanu

Malondatu awa TV ndi remote yake mupeleka zingati
21/08/2025

Malondatu awa TV ndi remote yake mupeleka zingati

Ndiye kuli nsapato izi, kudula kuposa salary yachigulu
21/08/2025

Ndiye kuli nsapato izi, kudula kuposa salary yachigulu

Rest in peace to the compassionate Judge Frank Caprio, who passed away at 89 after a battle with pancreatic cancer. Your...
20/08/2025

Rest in peace to the compassionate Judge Frank Caprio, who passed away at 89 after a battle with pancreatic cancer. Your fairness and kindness touched us all.

Amanu a Wendy Harawa akutukutsa nyimbo ya tsopano mawa lino titled Over and Over
20/08/2025

Amanu a Wendy Harawa akutukutsa nyimbo ya tsopano mawa lino titled Over and Over

Chakwera wazituluka za presidential Depate ati sakapanga nawo, mphekesela zikumvekanso kuti APM atha osapezekako chifukw...
20/08/2025

Chakwera wazituluka za presidential Depate ati sakapanga nawo, mphekesela zikumvekanso kuti APM atha osapezekako chifukwa akadali ku mangochi ngakhale debate iliko mawa lino

Mukamayenda chonde kumaona komwe mukupita, mwamuona mayi uyu zinamuonekelatu
19/08/2025

Mukamayenda chonde kumaona komwe mukupita, mwamuona mayi uyu zinamuonekelatu

Ife tangotelotu masana ano
19/08/2025

Ife tangotelotu masana ano

Akulu mukuwaonawo ndi a Samuel Chinecherem Ezeh aku Nigeria ndipo aswa record (Guiness world record) popanga dress ya fa...
19/08/2025

Akulu mukuwaonawo ndi a Samuel Chinecherem Ezeh aku Nigeria ndipo aswa record (Guiness world record) popanga dress ya fashion yomwe Ili ndi mikono yaitali kwambiri kuposa chovala chinalilichonse pano padziko lapansi.Mikonoyi ndiyotalika 50 metres.

Mkuluyu yemwe ndi Fashion designer komanso telala, wati khumbo lake tsopano ndilofuna kuti ayende maiko osiyana siyana kukaonesa chovalachi kuti anthu ambiri aone ndikuyamikira luso lake.

Akatu sikoyamba kuti ku Nigeria kuchoke munthu yemwe waswa record pa dziko lonse lapansi pakuti zaka zochepa zapitazo mtsikana wina anaswanso record yophika ma ola ochuluka kwambiri osapumila komanso kugona.

Kumalawi tizaswa record koma? Kapena spanner apange apply titha kuwina kumadyedweku😂

Address

Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Spotlight Waves posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Spotlight Waves:

Share

Category