
09/10/2023
Ulendo wa Chakwera okacheza ku Mozambique wabala zipatso zokuphya. Tikunena pano mdziko muno mwafika diesel wochuluka ma lita 1.9 million kudzera ku Nacala kuyenda pa njanji. Koma petro adakabwera be pa ma truck ndipo ndi khumbo lathu kuti lanye ayambe kudzera pa njanji yi.