Ambuye Konzani NJIRA ZANGA.

Ambuye Konzani NJIRA ZANGA. BORN AGAIN GROUP

26/12/2025

Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Felia Wilson, Victor Makawa, Macroud Mpan, Joseph Kalimbika, Vanesa Landford, Madalitso James, Jonathan J King, Fezia Shaibu, Annah Jendausiku

16/10/2025

KUKUMBUTSANA MALEMBA

M'mwemo ndinakhala pambari pake ndi kumtsiriza chifukwa ndinadziwa kuti sangakhalenso ndi moyo wake, atagwa, Ndipo ndinatenga korona wa pa mutu pake, ndi chigwinjiri cha pa nkono wake, ndabwera nazo kuno kwa mbuye wanga.15, Davide anaitana wina wa anyamatawo, nati, Sendera numkanthe. Ndipo anamkantha, nafa iye. 16, Koma asanafe, Davide adanena naye, Wadziphetsa ndi mtima wako; chifukwa pakamwa pako padachita umboni wakukutsutsa ndi kuti, Ine ndinapha wodzozedwa wa Yehova

2 SAMUELI 1:10,15-16📖🛌
Mwa chidule Sauli anadzipha yekha ataona kuti adani amupha anadzibaya ndi nkondo wake nyamata wake atakana kumupha.
Koma pamene ndikufuna ndigawane nanu mpakuti, Munthu wina pofuna kupeza kukondedwa ndi Davide anamuuza ngati wamupha ndi iyeyo, ndimaganizo woti Sauli amadana ndi Davide, Koma Davide anamupha wodzanena bodza uja, Anafa chifukwa chonena bodza kuti akondedwe.
Anthu ambiri timafuna tinene bodza kuipitsa azathu kwa mabwana kuti adzitikonda ife, ambiri amangidwa, afa, adwala, ntchito inatha, ma transfers, chifukwa cha bodza lathu.
Nde pali mabwana ena mumakondwera ndikumva nkhani za bodza, kuti mupereke chithu nde wina akuchemeleleni kaye, Nkhani ya Davide ndi Sauli tiphunzirepo kathu, nkhani ya uyu anadzamuuza Davide bodza itiphunzitsenso kathu kena mabodza amaphetsa la 40 limakwana. Muliponso anthu ena mumafuna kulowelera udani wa anthu ena womwe simukuudziwa zidzakutsalirani tsiku lina musamalowerere, Davide akumuuza munthu uja kuti wadziphetsa wenkha.
Mukhale ndi tsilu labwino nonse

16/10/2025

Big shout out to my newest top fans! Tapiwa Chiwaya

16/10/2025

welcome to my newest followers! Excited to have you onboard! Austin Limbikani Masulani, Mkowa Chris Wa Moves, Paul Peter, Ernest Kunjakuno, Kondwan Tchuma, Edith Nkhoma, Vncent Manduwi, Rose Mbexy, Isaac Alex, Sindzan Banda, Gimoh Shatter, Regina Bandawe, Chiya Busby Katengeza, Bee Cee, Yusufu Alisa, Geremu Smarxy, Dee Major David Bwoy, Dakeni Nguluwe, Shine De Guy, Alemayehu Desta, Loyce Josephy, Tamisha Kalolo, Dumi Triple, Luciano Stima, Mphatso Matias, Leonard Masitala, Moyo Moyo, Brenda Kanyama, Gilbert Fadwork, Chrissy Alisa, Damiano Khoma, Teleza Ngozo, Amos Peter, Dominic Ishmael Jee, Baydon Nyoni, Naumih Chikaonga, Bra Msangwe Maston Nyilongo, Fidesi Staniel, Dalitso Palian, Frank Ranky P Mankhangala, Thîdêh MW, Elvis Kenzel Banda

13/11/2024

*Ngakhale ukuvutika koma sudzakhala choncho mpaka kalekale ndipo limbikila chomwe ukupanga mulungu sataya wache one day adzayakha mapephero ako nakupatsa chosowa chako Amen!!!*

13/11/2024

Welcome to our newest followers! Excited to have you onboard! Lymon Leneck, Mayamiko Jemsi, Geoffrey Phiri Mulewa, Jane Allie, Somus Nyilongo, Christopher Chinoko, Flayness Moyo, Otiria Simon

26/08/2024

NDICHINTHU CHOWAWA KWAMBIRI KUKHALA MUNTHU OKHULUPILIRA NDIWA PEPHERO KOMA NYENGO ZAKO MKUMALIMBABE😭😭. MULUNGU ASINTHE NYENGO ZA MOYO WAKO 👏AMEN!!!👏

26/08/2024

Welcome to our newest followers! Excited to have you onboard! Alice Chalema, Charity Ofesi, Bridget L.M. Banda, Connex Ligowe, Vuvu Zama Z**i Tsweleba V, Sosten Chisomo, John Nyirenda, Reni Wa Mido, Emily Kamwendo, Why Bifetine, Raphael Chimpesa, Jãčøb ÑGømæ, Wanton Mw, Priscilla Raphael, Lusson Mathebula, Felta Philimon, Mary Wa Benard Favor, Eb Kamkoto Fanuel, John Mawindo, Joseph Chimela, Isihaq R T Ahmed, Amos Pakijin C. Luhana, Mike Nala, Ben Gondwe, Weremu Masiyano, Yohane Bonongwe, John Junior Ndhlovu, Komzy Luhana, Sarah Dzumani, Innossia Mungo, Sphon Lauren, John Limbani, Ñêñgêzwãyo Ñhlãñe, Malunga Ofatsa, Vava Yamlomo, Dreck Mw, Happy Chî, Malizani Ngong, Alice Kingsley, Amicable R Phiri, Jacqueline Noah, Lodgers Banda, Medeeh Medeeh Zuze, Chrispine Mwafulirwah, Philipina John, Stover Khanyiwa, Cent Cassim, Darlington Tasiana, Temmie Shabah, Sim Oplect

26/08/2024

Congrats to our new rising fans! Martha Caflower Kabag, Christina Gondwe

26/08/2024

Welcome to our newest top fans! Tapiwa Chiwaya

17/08/2024

Address

CHILIMBA
Blantyre

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Ambuye Konzani NJIRA ZANGA. posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Ambuye Konzani NJIRA ZANGA.:

Shortcuts

Share

Category