DPP YOUTH

DPP YOUTH To promote youths in Malawi to take part in politics inorder to develop this country. Mighty DPP only the biggest party ever Malawi had with visionary leaders.

2025 next year kukhala zinthu,tiyetsetse tonse tikhale ndi ziphatso za unzika komanso amene akukwanitsa zaka 16 kumene a...
22/01/2024

2025 next year kukhala zinthu,tiyetsetse tonse tikhale ndi ziphatso za unzika komanso amene akukwanitsa zaka 16 kumene akalembetse mwaunyinji kuti azavote Adad abwererenso pa mpando.

24/05/2023

Some people in DPP are asking the party president Professor Arthur Peter Mutharika to stand and compete at the party forthcoming convetion which will be schedule in July 2023,what is your reactions,is it a right decision to have APM on a ballot paper in 2025?

30/06/2022

Ma MP angapo akatenga chiletso choti Dr Chaponda atsagwire ntchito yawo ngati leader of opposition,iwo akuyikira kumbuyo ganizo loti Dr Nankhumwa apitilire kukhalabe mtsogoleri otsutsa boma mnyumba ya malamulo.

27/06/2022

Mighty DPP members of parliament has changed the leader of opposition post from Hon Kondwani Nankhumwa to Hon George Chapatula Chaponda,what is your final thought about the changes?

08/06/2022

Boma la Tonse likuti amene akudzudzula president Chakwera kuti atsamayendeyende ngati njira imodzi yopulumutsira chuma cha dziko lino ndi a CHULE Inu mwayilandira bwanji nkhani imeneyi?

How do you rembering him?
03/09/2021

How do you rembering him?

26/03/2021

DPP ngati chipani chotsutsa boma tikuchiona bwanji mphamvu zake zobweleranso m'boma mu chaka cha 2025 kodi chikulephera patino kapena mphamvu zake zili patino,ngati chili chofooka kapena ndi cholimba chikuyenera kutsintha patino kapena kulimbikira patino?

26/03/2021

APM mandate yake yokhala pa mpando ngati mtsogoleri wa DPP itha 2023 ndipo chipani chaganidza chozapangitsa convention mu July 2023 koma ena akufunitsitsa convention itachitika mwansanga,inu ngati masapota maganizo anu ndi otani?

11/03/2021

Ganizo loti onse ofuna udindo ku DPP ayambe atsiya campaign yawo yofuna u president mmalo mwake ayambe athandidzira ma candidate athu mmadera mosiyanasiyana mwalirandira motani kuti after zonsezo adzayambirenso?

08/03/2021

Ngati a DPP choyenera kuchita padakali pano ndi chani kuti chipani chathu chikhale cha mphamvu kuposa mmene chinalili mmene timapita ku chisankho chaka chathachi?

08/03/2021

Ku DPP ndi mtsogoleri uti amene mukuona kuti atha kutsogolera chipanichi kufikira kutenga boma pakati pa Dr Dalitso Dr. Dalitso KabambeDr. Dalitso Kabambe Dalitso Kabambe,Kondwani Nankhumwa,Bright Msaka,Joseph Mwanamveka ndi Cedrick Cedrick Ngalande?

Address


Opening Hours

Monday 06:00 - 12:00
Tuesday 06:00 - 12:00
Wednesday 06:00 - 12:00
Thursday 06:00 - 12:00
Friday 06:00 - 12:00
Saturday 06:00 - 12:00
Sunday 06:00 - 12:00

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when DPP YOUTH posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

  • Address
  • Opening Hours
  • Alerts
  • Claim ownership or report listing
  • Want your business to be the top-listed Media Company?

Share