Mviews

Mviews Welcome to M views

26/05/2024

Ma post tiyambano kupangira Kuno

26/05/2024

Cooking New Song

10/05/2023

Please don't Laugh

16/04/2023

Nkhani zankokomesya
Tiziyambepo🤣🤣🤣🤣

Reporter wankulu wa ku
Ali ndi mwana🥳🥳🥳

05/07/2022

Nkhan zankokomesyaaa

Nzimayi wina wa kunsanama mm'boma la Machinga wamusumira Landlady wake kupolice kaamba kakut amazemberana ndimamuna wake
Nkhani nkumati Landlady yu amafuna kulanda mamuna was tenanti wake

Koma asanapite kupolice ko mmbuyomu munali chindeu cha zawoneni ndikunena pano Landlady yo alibe dzino limodzi

31/05/2022

Kuchokera ku Mviews KHODO yemwe wakhala akuyimba tsopano wasiya kuimba
Thanks very much

27/02/2022

Mviews ikusangalala kubadwa kwa njovu ziwiri moti kwavuto ndi promotion

M views yapanga beat beat oyilowa ndi 3pin audio + video kwa amene musaowa ma vids mwati ndiwomweu
09/02/2022

M views yapanga beat beat oyilowa ndi 3pin audio + video kwa amene musaowa ma vids mwati ndiwomweu

09/12/2021

Ku Mviews kwakhala kukuchitika ma MIC🎙BATTLE komaso ma freestyle lelo tikhala tikuponya zimenezi kuti amene simunaone muzione kunalitu zithu

Catch Khodo (lisimba) pamene lero 8:30pm akhale live on Facebook on this page pamene akhale akuimba zina mwa nyimbo zime...
07/12/2021

Catch Khodo (lisimba) pamene lero 8:30pm akhale live on Facebook on this page pamene akhale akuimba zina mwa nyimbo zimene inu zimakusangalani # NDAKUPASA COVER BASI COVER ndi dzina zambiri tisaiwale kuti khodo ndi producer , camera man komanso ndi oimba
Hosted by Sparta
and like the page

19/11/2021

Morning people

Address

Namwera
Blantyre

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Mviews posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Mviews:

Share

Category