
01/10/2024
*Pilex tablets plus Heamorrhoids spray weapons to cure piles, Heamorrhoids*
Anthu ambiri mbiri amakhala akudandaula pa nkhani ya pobibira.
✓Ena amatulutsa magazi Kobibira.
✓Ena kutuluka sungu Kobibira
✓Ena kumva kuyabwa Kobibira
✓Ena kukanika kubiba ngati Kuli ulimbo.
*Solution ya zonsezo*
Pezani pilex tablets ndi Hemorrhoids spray 💯 Guarantee.
👉Amachiza kuyabwa yabwa Kobibira.
👉 Kuchotsa sungu Kobibira
👉kuchiza matenda otulutsa magazi Kobibira.
👉Kuchiza kupweteka Kwa Kobibira.
👉Kuchiza Likango, Heamorrhoids la mkati.
👉 Amachotsa kunanda komanso kumata Kwa Kobibira.
👉Amachiza kufufuma(swelling) Kwa Malo obibira.
👉 Amachotsa zilonda zomwe zimamata Kobibira (sungu).
*Mamwedwe Ake alipo monga*
✓Tengani ma tablets awiri morning and evening awiri a pilex tablets.
✓Hemorrhoids spray, zoletsani pomwe Pali Likango, Heamorrhoids po morning and evening.
Tinene Panopa mosindika*
Ma herbs amenewa amachiza Likango, Heamorrhoids. 7 days umakhala waona kusintha kenako bas kuchiriratu🙏
Pilex tablets k15,000*