
19/06/2025
Pa ma missile 10 omwe inaponya Iran chapompano, 4 afika pa ground ndipo apweteka ma buildings angapo ku Israel kuphatikizapo Soroka Hospital in Beersheba, Southern Israel.
Bomba lina lakapweteka Stock Exchange ku Ramat Gan, East of Tel Aviv ndipo ena awili agwetsa ma buildings akulu akulu ku Israel.
Zikuveka ngati ma siren amabombawa sanaveke muja akumachitila, angozindikira kwayipa. Bomba lomwe lagwela ku chipatala lapangitsanso ma hazardous chemicals from the hospital to leak.