Mervin Kambani's Diary

Mervin Kambani's Diary PATSINDE🧭🏝πŸ’₯πŸ’«
FOLLOW THIS PAGE FOR MORE FUN

Eeeee anzathu 😌😌😌 oziwa malamulo adziko
05/05/2025

Eeeee anzathu 😌😌😌 oziwa malamulo adziko

amene munabadwa kale ,, nndani uyu???
01/05/2025

amene munabadwa kale ,, nndani uyu???

LIKAWALA DZUWALO β˜€οΈ Ndidziwa ndinu ambuye mwateloSimulora utsiku kukhala amoyo wanga matheloLikawala dzuwaloMdima uthawa...
26/04/2025

LIKAWALA DZUWALO β˜€οΈ

Ndidziwa ndinu ambuye mwatelo
Simulora utsiku kukhala amoyo wanga mathelo
Likawala dzuwalo
Mdima uthawa
Timva kulira Kwa mbalame mlengalenga
Ndipo ndidziwa zonse ndinu mukonza namalenga
Likawala dzuwalo
Lindipatsa phunziro lalikulu
Kuwala kuthawitsa mdima
Ndiderenji nkhawa ngat mavuto sangathe
Likawala dzuwalo
Pemphero ndiponya kwa Inu atate
Ndipo ndidziwa ndekha simungandisiye πŸ™

(MERVIN'S DIARY POEMS)

09/08/2024

Pa boma πŸ’ͺ

Address

Blantyre

Telephone

+265995120050

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Mervin Kambani's Diary posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Mervin Kambani's Diary:

Share