Mikoko

Mikoko Mikoko Entertainment is Malawi's fastest growing Brand (Award winning Media)

Based in Blantyre, Malawi 🇲🇼

Be part of our Journey 👫

29/05/2025

Nkazi wanga dzuro anatora 30 pin ndi nsalu,lero watora nyama 4kg ndi mafuta ophikira 2litres' anabadwa ndi mwayi nsaname

29/05/2025

Nkhani yavuta ndiya Ma Chisomo 🤣

Big shout out to my newest top fans! 💎 Precious Biton Banda, Squeeser Mw, Elyna Tembo, Męrvyñ Kíñgkåtãkwé Ćhīlãpùlã, Hap...
26/05/2025

Big shout out to my newest top fans! 💎 Precious Biton Banda, Squeeser Mw, Elyna Tembo, Męrvyñ Kíñgkåtãkwé Ćhīlãpùlã, Happy Mtambalika, Blessings Kaliapa, Andy Ndugdzai, Chisomo Taulo, Patrick Pkd Mbewe, Foster Chikondwa

Drop a comment to welcome them to our community

22/05/2025

Big shout-out to my newest top fans! Precious Biton Banda, Squeeser Mw, Elyna Tembo, Męrvyñ Kíñgkåtãkwé Ćhīlãpùlã, Happy Mtambalika, Blessings Kaliapa, Andy Ndugdzai, Chisomo Taulo, Patrick Pkd Mbewe, Foster Chikondwa

SKC legacy writes;Tikhoza kusiyana chipembezo, ndale kapena mtundu koma umunthu is what defines a man. Ngati imfa ya win...
05/05/2025

SKC legacy writes;
Tikhoza kusiyana chipembezo, ndale kapena mtundu koma umunthu is what defines a man. Ngati imfa ya wina ake sukukhudzika nayo asiyeni omwe ali pachisoni alire mpaka pomwe atathere osati kuyamba kuwanyoza.

Imfa ya SKC bambo Chikumbutso Mtumodzi anatinyoza akuti "mukuliratu kwambiri maliro a Chilima, kodi kadali kamulungu kanu kuti sangafe." Pope Francis atamwalira he commented on a certain post kuti wasala APM nayeso wakalamba akuyenera kufa.

Ma Bishop akangoyankhulapo anything to do with government ndiye amanyozedwa momvetsa chisoni.

And today, Mr Chikumbutso Mtumodzi is no more, Kodi abale ake akamalira zikhala kuti iwowa anali kamulungu kawo? APM uja amati akuyenera kufa uja is so strong ku Mangochi uko.

Osamatha mau, Rest in peace Chikumbutso Mtumodzi 🕊️

05/05/2025

Ma producer ochotsa ma tag pa beat yopanga download ulemu wanu 🤣

02/05/2025

Mwaswera bwanji pa mudzi pano

24/04/2025

Big shout-out to my newest top fans! Precious Biton Banda, Squeeser Mw, Elyna Tembo, Męrvyñ Kíñgkåtãkwé Ćhīlãpùlã, Jay Dilla, Happy Mtambalika, Blessings Kaliapa, Andy Ndugdzai, Chisomo Taulo, Patrick Pkd Mbewe, Foster Chikondwa

24/04/2025

Mwaswera bwanji pa mudzi pano?

11/04/2025

We're poor because when it is raining we think about s*x instead of planting crops 😢

11/04/2025

Nowadays they don't bewitch you to go crazy. They just make sure you drink alcohol whenever you have money.

Good morning

08/04/2025

Zimafunika kumalimbikira uku ukupemphera osati kumangopemphera utangokhala, umati zichokera kuti🥺

Address

Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Mikoko posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category