21/03/2023
New Beat Running on Our YouTube Channel titled
Pop Young X Driemo Type beat
Mix miyezi imeneyi tamvera kwambiri Mesa ndi Pano, mudziwa kale ka insipiration kutigwira basi tapanga kameneka ๐
Check Out ka snippet kake below!! full beat link in the comment section
Osaiwalla kupangirako Subscribe and Like youtube channel
Zikomo.