Mvungi Job Master

Mvungi Job Master Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Mvungi Job Master, chilomoni, Blantyre.
(9)

Mvungi — All-in-One AI-Powered Platform | Job Automation | Intelligent Matching | CV Optimization | Career Opportunities | Recruitment & HR Management | Business Document Solutions | Malawi-Built Innovation

10/06/2026

Awatu mupange apply awa. Ngati anu palibe, aitaneni anzanuwo avunge👇

What every HR Manager wishes they had:✓ Employee records in one place✓ Automated leave approvals✓ Attendance tracking✓ I...
10/06/2026

What every HR Manager wishes they had:

✓ Employee records in one place
✓ Automated leave approvals
✓ Attendance tracking
✓ Instant HR reports
✓ Recruitment tracking
✓ Payroll integration
✓ Workforce analytics

With Mvungi Job Master, wow you can.

Mvungi Smart HR Manager is a complete workforce management platform designed for Malawian organisations, SMEs and industries.

Book your free demonstration today.

Lero pa 10 June ndi tsiku lomwe Malemu Dr. Chilima ndi anthu ena 8 anatisiya pa Ngozi ya ndege ku Chikangawa mu chaka ch...
10/06/2026

Lero pa 10 June ndi tsiku lomwe Malemu Dr. Chilima ndi anthu ena 8 anatisiya pa Ngozi ya ndege ku Chikangawa mu chaka cha 2024💔

May Their Souls Continue Resting In Peace🕊️

09/06/2026

Two weeks ago we had 7K users. Times, MIJ and Capital FM atalemba impact yathu, anthu oposa 9K tsopano akugwiritsa ntchito Mvungi 🔥🔥

09/06/2026

Mukakhala ndi account ya Mvungi, mumatha kuona ngati application yanu yawerengedwa ndi employer kapena ayi.

09/06/2026

Sikuti makalata safika. Koma pena CV yathu simawadalitsa. Tayesani Mvungi ikuthandizeni. Anzanu akupindula🔥

09/06/2026

Apply the vacancies now! Sometimes later becomes never 😒

Apa Mvungi yabwera basi🔥🔥🔥 Ena akumapepusabe😂😂😂Tsegulani account inu tizikupangirani apply ma vacancy wa.
08/06/2026

Apa Mvungi yabwera basi🔥🔥🔥 Ena akumapepusabe😂😂😂
Tsegulani account inu tizikupangirani apply ma vacancy wa.

08/06/2026

Anthu ambiri akuti feature yoti aziziwa ngati email yawo employer waisegula ija taiganiza bwino 😁 tiphunzira kulimba mtima bas😉

Address

Chilomoni
Blantyre
312212

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Mvungi Job Master posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share