09/08/2025
Mwayi! Mwayi! Ndikutitu chi mwayi!! π₯
Maranatha ndiyokondwa kukudziwitsani makolo komanso ophunzira nonse omwe muli ndikuthekera.
Maranatha yapeleka mwayi okuti ophunzira akhoza kumakaphunzira ku university yaikulu ku India yomwe imatchedwa kuti Sharda University komwe ku India.
Ndipo ukuku Kuli mwayi wama scholarship, omwe azikachitikira kunjako komanso kwa ana omwe akufuna kuyamba Secondary, Inu ndikuti kuyambira Form 1 mpaka 4, komwe akaloledwe kulembetsa opanda entrance exams komanso registration is FEE!, Aah inu mwayi uposele apa??
Mwambo onse ukachitika motere;
Malo: Sun Bird Mount Soche ku Blantyre.
Tsiku: 12 August 2025 Tuesday
Nthawi: 8AM - 5PM
Contact them on: π
0990980077
0888848888
0999679736
0999611755
NDIKUTITU NDIZAULELE!!!
Makolo ndi banja lawo apite uku, zambili zokhuza Maranatha Academy ndi University yaku India mukazimvele ku Hotel.
Aiponyela Kutalitu, Ndikakhala ine mukandipeza komweko ndi Ana anga!.