Malawian news summaries

Malawian news summaries nkhani zosiyanasiyana zapa malawi Ndife Amalawi ozindikiraso
(1)

12/04/2024
11/04/2024

VACANCY ANNOUNCEMENT@ NDEKELIRE INVESTMENTS

POSITION: DRIVER

Location: Zomba

JOB DESCRIPTION
An opportunity has risen at Ndekelire investments. Ndekelire investments is a Malawian company located in Zomba.

Location: Zomba

DUTIES AND RESPONSIBILITIES Perform minor vehicle mentainances Baggage: Safely transport either cargo or passengers from one location to anotherplan routes and meet delivery schedulesCollect payments and Issue receiptsDeliver Excellent customer serviceDocument distance travelled and keep receipts Regularly washing and cleaning the vehicleMaintain Vehicle mileage logs.Performing inspections of vehicle and equipment Demonstrate Safe driving practices Ability to follow traffic rules and follow accident procedures.

COMPETENCIES Completion of secondary school Education. A post Secondary Certificate in motor vehicle mechanics (grade 3) will have an added advantageA clean SADIC class C1 driving License Minimum of 3 years of relevant work experience as a driver with safe driving record Knowledge of driving Regulations, Rules and laws as well as skills in minor vehicle maintenance Adequate Communication skills to be able to liase with Police and Protocol Staff on different assignments Fluency in English and ChichewaMust be between 40-45 years

MODE OF APPLICATION
A completed application letter, copies of nation ID and driver's license and a curriculum Vitae with 3 traceable referees should be sent to [email protected] not later than 30th April 2024.

Female applicants are to apply. Only shortlisted candidates will be contacted.

16/03/2024

Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Leo Nkasala, Graciano B WA, Eric Ngulama, Mbang'ombe Mcbarnet, Tolonto Kondowe Chidumayi, Enock Mawira, Witison Afack, Paul Mdeza, Bize Mandime, Imrani Kam'mwamba, Henry Nyirongo, Soldiers Stenala, Lemison Suliali, Felix Ochukumba Nseula, Joseph Mkata, Mostapher Fam Banda, Sidcane Gt

Nthambi yoona za anthu olowa ndi kutuluka m'dziko muno yati yamaliza kukonza makina opangira ziphaso omwe anaonongeka m'...
13/03/2024

Nthambi yoona za anthu olowa ndi kutuluka m'dziko muno yati yamaliza kukonza makina opangira ziphaso omwe anaonongeka m'mbuyomu.

Malingana ndi chikalata chomwe nthambiyi yatulutsa ndipo wasayimira ndi mkulu wake Brigadier General Kalumo, chati nthambiyi tsopano yayambiranso kupanga ziphaso ndipo ntchitoyi iyambira kaye m'boma la Lilongwe lisanafike pofalikira maboma ena.

Chikalatachi chatinso boma tsopano latsitsa mtengo opangira ziphaso kuchoka pa MK 90,00 kufika pa MK50,000 ndipo anthu azitenga ziphasozi m'masiku khumi.

12/03/2024

Chipani cha UTM chati mgwirizano wawo ndi MCP pa yemwe akudzaimira mgwirizano wa Tonse mu chisankho chikudzachi sudasinthe ndipo ‘udakali chimodzimodzi’.

Mlembi wamkulu wa UTM, Patricia Kaliati, watiuza kuti adagawana zaka zisanu kwa otsogolera aliyense ndipo kuti mfundoyi sidachitike ndi atsogoleri a zipani ziwiri zokhazi ayi koma kuti otsatira ena adavomereza.

Malingana ndi Kaliati, mgwirizanowu ukudzaimiliridwa ndi mtsogoleri wa UTM, Saulos Chilima, pa chisankho cha chaka cha mawa popeza kuti mtsogoleri wa MCP, Lazarus Chakwera wachita kale mbali yake.

Izitu zikudza patapita sabata komiti yaikulu ya MCP itanena kuti odzaimila chipanichi mu chisankho chikudzayi ndi President Chakwera.

Poyankhurapo, katswiri pa ndale George Phiri wati kusainila mgwirizano kwa atsogoleri a mu mgwirizano wa Tonse kumaimila zipani zawo ndinso kuti MCP kusakha mtsogoleri wawo mu 2025 kukhoza kukhala mbali imodzi yokwaniritsa za mgwirizanowu.

12/02/2024

Feel good music

11/02/2024

Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Leffan Byssaln, Thomas Amakabeo, Takayo Tekken

BLANTYRE BLUE CONVOY Tsiku:  4 FebruaryKonyamukira: Southern Region OfficeNthawi: 9 koloko mmawa09:00 Start offRoute➡️Ch...
04/02/2024

BLANTYRE BLUE CONVOY

Tsiku: 4 February
Konyamukira: Southern Region Office
Nthawi: 9 koloko mmawa

09:00 Start off

Route
➡️Chilomoni Sigelege
➡️Chilomoni Nthukwa
➡️Ndirande market kudutsa kuma flat
➡️ Ndirande Chimsewu
➡️Mbayani pa Clinic ya Sonkie kudzera BT city
➡️Chilimba pama Land Rover
➡️ Machinjiri Luwanda
➡️ Machinjiri Chikapa
➡️ Machinjiri Khama
➡️ Kachere
➡️ Limbe kumsika
kudzera Kanjedza
➡️ BCA
➡️ Bangwe Mvula
➡️ Bangwe Post Office
😪➡️ Namiyango Ring Road (Route back to Midima Rd)
➡️ Manje (Mini rally)

NB: this route is subject to change

01/02/2024

VACANCY ANNOUNCEMENT@ MALAWI SUN HOTEL

POSITION: FRONT OFFICE MANAGER & RESTAURANT CASHIER

Location: Blantyre

Front Office Manager
Restaurant Cashier

APPLY NOW
Please send your application letter and Curriculum vitae to the below email address before 5th February 2024

Email: [email protected]

Bangwe- Machinjiri - Kachere- Ndirande- Nkolokosa - Zingwangwa - Mbayani -Chilomoni - Mpemba - Chirimba - Kameza - Chile...
30/01/2024

Bangwe- Machinjiri - Kachere- Ndirande- Nkolokosa - Zingwangwa - Mbayani -Chilomoni - Mpemba - Chirimba - Kameza - Chileka - Lunzu ndima township onse azayaka 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥

Address

Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Malawian news summaries posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share