92 Media

92 Media we are a promo platform

Promo
Event host 101🔥💯🎄 92media Dynasty here and beyond
(9)

Akutitu Presidential Swag😂😂😂
19/07/2025

Akutitu Presidential Swag😂😂😂

Zimitsa gesi
18/07/2025

Zimitsa gesi

UWU NDI MWALA OMWE UNATENGEDWA KU PLANET MARS NDIPO WAGULITSIDWA PA KUSHONI PA MTENGO WA $5.4MILLION YOMWE KU MALAWI KUN...
17/07/2025

UWU NDI MWALA OMWE UNATENGEDWA KU PLANET MARS NDIPO WAGULITSIDWA PA KUSHONI PA MTENGO WA $5.4MILLION YOMWE KU MALAWI KUNO NDI MK8,670,674,850.00. AZUNGU CHOMWE AMAFUNA ADZACHIPEZA NDITHU

NAYE DOKOTALA AMAFUNA MOYO
17/07/2025

NAYE DOKOTALA AMAFUNA MOYO

Nkhani ikutero kuseliku🤣🤣🤣
17/07/2025

Nkhani ikutero kuseliku🤣🤣🤣

GAME YOWAWA KWAMBIRI KWA ANTHU OKUNGA MA TICKET...MAKOBILI APITA NDITHU.
14/07/2025

GAME YOWAWA KWAMBIRI KWA ANTHU OKUNGA MA TICKET...MAKOBILI APITA NDITHU.

Donald ati walema naye Putin ndipo amuonetsa mbwaza akadeleranso
10/07/2025

Donald ati walema naye Putin ndipo amuonetsa mbwaza akadeleranso

Ma stunt aukali
10/07/2025

Ma stunt aukali

ANTHU OKONDA ZA NDALEWA akuti amene anali wachiwiri kwa msogoleri wa dziko lino a Everton Chimulirenji atuluka DPP ndipo...
09/07/2025

ANTHU OKONDA ZA NDALEWA akuti amene anali wachiwiri kwa msogoleri wa dziko lino a Everton Chimulirenji atuluka DPP ndipo pa dzisankho za mu september zikubwerazi ayima pa u MP ngati membala oyima payekha kamba koti ku DPP ko iwo sakuonako za chilungamo zolongosoka, akuti akukhomeleredwa ndikudyeredwa masuku pamutu

Jota sadaikidwe mkomwe m’manda koma azimayi kuno ku Africa ayamba kale kukambilana, ati: ‘Kodi chuma cha Jota achiyendet...
05/07/2025

Jota sadaikidwe mkomwe m’manda koma azimayi kuno ku Africa ayamba kale kukambilana, ati: ‘Kodi chuma cha Jota achiyendetsa bwanji? Mkazi wake alandira zingati?🙌eeeh

Galimoto simasankha driver, koma driver ndiamene amasankha galimoto 😁 Good morning, kwacha?
05/07/2025

Galimoto simasankha driver, koma driver ndiamene amasankha galimoto 😁 Good morning, kwacha?

Address


Opening Hours

Monday 09:00 - 17:00
Tuesday 09:00 - 17:00
Wednesday 09:00 - 22:00
Thursday 09:00 - 17:00
Friday 09:00 - 17:00
Saturday 09:00 - 17:00
Sunday 09:00 - 17:00

Telephone

+265884358502

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when 92 Media posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to 92 Media:

Shortcuts

  • Address
  • Telephone
  • Opening Hours
  • Alerts
  • Contact The Business
  • Claim ownership or report listing
  • Want your business to be the top-listed Media Company?

Share