Nsanje Post

Nsanje Post Political News Updates | Trending news.
(3)

    Yafa⚽ ngati bodza🫪🤔
30/05/2026


Yafa⚽ ngati bodza🫪🤔

  Mwambo oika Thupi la bambo MuonjaBambo ake Mbuya Antonyo Comedian
30/05/2026


Mwambo oika Thupi la bambo Muonja
Bambo ake Mbuya Antonyo Comedian

  in Peace 🕊️Pepani   Antonio 😭Bambo wake Mbuya Antonyo Comedian Atisiya dzulo pamene amadwala kuchipatala,👂Aikidwa M'ma...
30/05/2026

in Peace 🕊️
Pepani Antonio 😭
Bambo wake Mbuya Antonyo Comedian
Atisiya dzulo pamene amadwala kuchipatala,

👂Aikidwa M'manda lero kwa Tengani ku Nsanje

    wakale wa dziko lino His Excellency Dr. Lazarus McCarthy Chakwera yemweso ali mtsogoleri wachipani cha Malawi Congre...
30/05/2026


wakale wa dziko lino His Excellency Dr. Lazarus McCarthy Chakwera yemweso ali mtsogoleri wachipani cha Malawi Congress Party(MCP),pamodzi ndi mayi wakale wapfuko lino, Madame Monica Chakwera,lero Loweluka pa 30 May,2026, akakhala nawo pa mwambo woyika m'manda m'bale wawo wa Madame Monica Chakwera m'boma la Nkhatabay.

Kotero mamembala omwe ali m'bomali ndi madera ozungulira akupemphedwa kukamukuta President Chakwera komanso Madam Chakwera pamene akakhale akupeleka ulemu wawo womaliza pa imfayi.

Congratulations New Minister Of Mining  . Thoko Tembo
30/05/2026

Congratulations New Minister Of Mining . Thoko Tembo

HIP HOP WADWALAget well soon IKK Oyimba zachinyamata yemwenso amadziwika kuti   HOP wadwala Ndipo sizikudziwika Chomwe A...
28/05/2026

HIP HOP WADWALA
get well soon IKK
Oyimba zachinyamata yemwenso amadziwika kuti HOP wadwala Ndipo sizikudziwika Chomwe Akudwala,

Happy birthday Bwana👏Dr Namadingo Tikudikira 2030 paja munati Chinthuchi mukutenga basi🔥🫪
28/05/2026

Happy birthday Bwana👏
Dr Namadingo

Tikudikira 2030 paja munati Chinthuchi mukutenga basi🔥🫪

28/05/2026

Interview 🎙️
. Ben Phiri
of Local Government
BOMA likufuma likuze msewu wa M1 ndichifukwa chake tawachosa ochita malonda pa WAKA WAKA Market 🫪

Ndalama za CDF Tionesesa kuti zikugwira ntchito yake bwino bwino opanda osolorapo🔥👏

Big man amatha Kucheza 👏🤔 Happy birthday Bwana   SulugweMwini wake wa Akometsi
28/05/2026

Big man amatha Kucheza 👏🤔
Happy birthday Bwana Sulugwe
Mwini wake wa Akometsi

27/05/2026

Precious Kabambe 🇲🇼

zomwe Walankhura Shadow MP wa MCP Lilongwe Bwaila constituency pamene akukonzekera kupita kuchisankho Cha Chibweleza .....

uyu chinthuchi achitenga ndithu 🔥🔥

Cabinet Meeting at Kamuzu Palace    Peter Mutharika
27/05/2026

Cabinet Meeting at Kamuzu Palace

Peter Mutharika

Address

Blantyre

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Nsanje Post posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share