Gerald Dzimbiri Mw

Gerald Dzimbiri Mw the ground of malawian gospel music . that can change u from the world to de heaven

31/08/2023

Lero sindikukhalitsa pa line kmabe tiyeni tilankhulane pa wapp. +258869909553

https://www.afrocharts.com/song?id=4824ef2134
19/12/2022

https://www.afrocharts.com/song?id=4824ef2134

Amapiano Wedding song by Grace Anankhoma Mataka - AfroCharts Buy & Sell, Stream & Download African Music for Free on AfroCharts - Free MP3 download, African Music Charts, African Artists, African Songs, Playlists

Alhomwe okhaokha azipanga zawo .majokosi okhaokha
09/12/2022

Alhomwe okhaokha azipanga zawo .majokosi okhaokha

  Gerald Dzimbiri Mw  Ndumufunira zabwino zonse pomwe wayamba 4m 4 .My first Daugher .mai Anga. .kukula mwathazi ndi Mze...
19/10/2022

Gerald Dzimbiri Mw Ndumufunira zabwino zonse pomwe wayamba 4m 4 .My first Daugher .mai Anga. .kukula mwathazi ndi Mzeru .God bless you Dota🕊🕊🕊🕊

27/08/2022

I feel full video💪💪💪💪💪💪💪💥💥💥

28/05/2022

Tamvetserani abale anga,

Pamalo poti Pali chisangalalo ndipo Pali anthunthu ambiri mbiri komanso anthu otchuka okha okha .Moto nkudzayaka mchigulu momwemo komwe wachokera Moto kosaziwika anthu nkuyesetsa nkupulumutsa mzawo nkumutulutsa wamoyo ndithu mwini wake atalezeleratu modetsa nkhawa .koma oyimba Mulungu azikudalitsani kwambiri ndipo Mulungu azikudalitsani mwaonetsa mtima umodzi koma Ambuye ndi omwe akomza izi osati munthu ayi.

Achipatala nawo nkudzagrwira ntchito yawo koma nje zosatheka imfa mpakana nayo nkudzaluma Mano eish Gentlemen tiyeni tizikhala opemphera ndi okomzeka nthawi zonse nkutheka ichi chitha kukhala chithumzi thunzi Cha gahena chabe koma mzathu Matse Nkukalowatso kumoyo otsatha Bobo ndithu

Koma nanga otsalafe omwe timazithi ndife otchukafe, takomza njira zathu Kodi?

Nanga ifeyo amene sitinatchuke koma tamva imfa za anthu otchuka ambiri Kodi Tamapempheradi mchoona?

Titengerepo phumziro kuti kutchuka sikanthu koma kukomza njira zathu basi mu Dzina la Yesu nkhrist .Osamaziyenereza oyimba inu osamaziyenerezanso omvera inu Moyo uno siwathu ndi was mwini anatilengayo.

Ndipemohere

Ambuye dalitsani yemwe wamva uthenga uwu komanso mukhululukire machimo nga ndi ake omwe pompano mundikomzenso kuti ndikhale mwana want watsopano . Ine vigololo ndileke Amen

Amen

11/04/2022

Ndimakonda onse ondikondanso .
Osandikondanso ndimawa konda thats why sindimavutika😎
I study Life with my Hamble🤣🤣🤣🤣

King Mcdougal
06/04/2022

King Mcdougal

19/03/2022

Gospel Music promo & Music Journey ikupusha

Awa ndi Pastor favour omwe anayimba nyimbo ija yomwentimati ndipo after kudziwana kwa kanthawi kochepa nawonso nkudzapeza mwayi okacheza ku SABC

Oyimba omwe muli ndi malutso mukuwabisa plz bumbulukani .pokuti Zutheka ndithu ndi Amnuye .

Pastor Favour kapena kuti Favour Thomson ndi munthu mozi Yemwenso alinawo mu ya Gospel music promo Network Company

Yomwe panopa yayamnika ndi anthu khumi .

Monga awa:



Sir


Grace Mataka (Anankhoma)



Maliro jnr



(Apex beats from Real sounds studio)



Komanso Favour Thomson

Ndipo bwana Thomson ndi awa akupita ku SABC💥💥💥💥💥💥💥💥💥💥💥💥

Thank you so much Anankhoma mataka the company will Come Great💥💥 and power

Address

Blantyre

Telephone

+258846032936

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Gerald Dzimbiri Mw posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share