Malawi Eye

Malawi Eye Malawi Eye is an online media group.

Koma Phwedoyu bwanji?
18/07/2025

Koma Phwedoyu bwanji?

Why disabling the comment section asking for a friend?
27/03/2025

Why disabling the comment section asking for a friend?

RIP Lucius Chiccio Banda 😭
01/07/2024

RIP Lucius Chiccio Banda 😭

Copied from Zodiak Online   Anthu okhala dera la Majiga ku Balaka ayamba kuchita m'bindikiro pa ofesi yogulitsa magetsi ...
19/03/2024

Copied from Zodiak Online

Anthu okhala dera la Majiga ku Balaka ayamba kuchita m'bindikiro pa ofesi yogulitsa magetsi ya ESCOM ati kufikira atawakonzera magetsi kuderali.
Anthuwa, omwe adapereka kalata yopeleka maola 24 ku bungweli sabata yatha kuti awakonzere magetsi omwe akhala asakuyaka kwa mwezi tsopano, atchingira ogwira ntchito kuti asalowe kapena kutuluka ku ofesi-zi.
Zokambirana zatenga maola angapo tsopano pakati pa atsogoleri a anthuwa ndi ena mwa ogwira ntchito ku ESCOM-ku.

06/11/2023

Thank you for the support you always give us. Lets grow together.

Address

Blantyre

Telephone

+265888857520

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Malawi Eye posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Malawi Eye:

Share

Category